01/09/2022
Ackleo Sakala
Yung Rich Nigga
01/09/2022
Koma lero ni lero mawa nimawa koma sinikakhala mawa
20/07/2022
DZIWANI IZI AKAZI INU
π©βπ¦°π©βπ¦°π©βπ¦°π©βπ¦°π©βπ¦°π©βπ¦°π©βπ¦°π©βπ¦°π©βπ¦°π©βπ¦°π©βπ¦°
Take Note:;
Pali akazi ena akamakhala amaganiza kuti iwowo akhoza kupeza banja chifukwa choti amatchena kwambiri ndipo anadalitsidwa ndi kuyela.
Ndiye pazifukwa izi akafunsilidwa ndi mwamuna amayamba amuyan'gana kaye mwamunayo kuti kodi ali ndi chani? Amapanga chani? Kodi ndiwantali kapena wanfupi? pamafunso onsewa akaona kuti mamunayo sakumatcha amayamba kumunyoza kumatukwana ati siwe type yangaπ
Akazi ambiri amaganiza kuti mwamuna akhoza kuwakwatira chifukwa choti iwowo ndiokongola kwambiri kapena ali ndi mahip abwino.
Uthenga nawu azimayi, mwamuna wanzelu zake samakwatira mkazi chifukwa cha mahip, kuyera kapena kutchena ayi izi zimangothandizira kuti tikufunsileni basi koma tikakukwatilani timafuna khalidwe lanu osati mahip, mahip ndi kuyelako zimafika potikwana chifukwa timaziona daily koma khalidwe labwino silitopetsa.
Zimadzapezeka kuti zaka ndikumadutsa mkaziyu mwamuna wa banja osamupeza, sikuti amunawo samamufunsira ayi koma amunawo amati akafika ndikuona khalidwe la mkaziyu okha amangososola sosola akatelo giya kuthawa ma demand.
Ndiyankhule chonchi
ππ½ππ½ππ½ππ½ππ½ππ½ππ½ππ½
Amuna amapanga chibwezi nthawi zina ndi zolinga ziwili basi, LOVE and S*X. koma ikafika nthawi yopanga chisankho chokwatla samayang'ana zimenezi koma amayang'ana .
Ndilongosole chonchiπ
( mwamuna atha kukukondani koma osadzakukwatlani.
( mwamuna atha kumagona nanu kwa nthawi yaitali koma osadzakukwatlani.
Ndipo mosayembekezeleka amazangopeza nkazi wina nkumukwatla.
Amuna ndi a tsogolo kwambili maka akafika pankhani ya kukwatila, samaganiza za velo, chinkhoswe kapena hall yomwe kudzachitikle chikwati ngati momwe akazi ambilinu mumaganizla kuti zimenezo ndiye kukwatiwa poti ndi zomwe ambili mumakhumba.
Mwamuna amazifunsa Kod mkaz yu azandisamala komaso ana ndabale anga?
Like my page Kuti mudziwe zambiri zakuchipinda
Share to 5 groups
Click here to claim your Sponsored Listing.
Location
Category
Website
Address
Matero