11/08/2025
It is elections campaigning season in Malawi. What is amazing me and many others out there is that every party is advising people to go and "vote wisely"...... akuti "mukavote mwazeru."
Kodi kuvota mwazeru ndekutani?
In these elections, kuvota mwazeru ndikuvotero posayang'ana chipani, chigawo, mtundu kapena chizoloweni.
Nde tiyang'ane mfundo kuti amene akunenako zomveka malingana ndi mavuto omwe dzikoli likukana nawo.