Musandide ine DN Hr ms

Musandide ine DN Hr ms

Share

Get nice story

29/04/2026
Photos from Musandide ine DN Hr ms's post 20/03/2025

Still available you can whtspp me
0679968213

Photos from Musandide ine DN Hr ms's post 15/03/2025

U can whtspp me if ur interested this
0679968213 we talk for more information

Photos from Musandide ine DN Hr ms's post 13/03/2025

Selling good curtains for good
price on special πŸ‘Œ

Photos from Musandide ine DN Hr ms's post 13/03/2025

Nice bedding set 5pic only
R299 u can whtspp on if u interested
0679968213

Photos from Musandide ine DN Hr ms's post 12/03/2025

Selling gud price u can whtspp me if ur interested 0679968213

Photos from Musandide ine DN Hr ms's post 16/11/2022

Right by Dan wa haroon plz flow the page ✍✍✍✍✍ kufika apapa ndakomana nazo sichibwana ai km kumbali yanga ndimathokosa mulungu pondisindila Nyengo dzanga.. mwa anthu ochuluka amaganidza ngati nchuma ichi ndichagadzi km ai ndikulimbikila kwanga bs ndiposo ena ndikamaudxa kuti ndagulitsako madzila ndochi masuku ndizina zotero km paka pano Samakhulupililabe km chachikulu ndikukhulupilila mulungu ndithu kt mulungu ndie ndamene amasintha Nyengo zamunthu aliyese ..
Km chimene chimafunika ndikulupililo ndikulimbikala bs km ineo chinthu chimoz ndichime ndinali ndinabe mtima odalila km kulimbikila basi penapake mtima odalila siwabwino umangoononga nthawi pachabe malo moti upuche mwawenkha uku ukudikila kt mulungu apanga nawe chani mukulimbikila kwako kwaineo or anthu atanena motani ndimakhala ndilibe nazo nchito coz chilungamo ndikuchiziwa ndekha kuti ndikuchokela pati....
Km Pena umbawi umakupangitsa munthu kuganidza wrong ichi ndifukwa anthu ambili amalowelela chimene amafuna nditendele wadzachuma kt apedza zosowa dzawo km kunena zoona ndalama ndiyofunika ndthu ichi ndichifukwa anthu amakhala ali yakaliyali kufuna zinchito kmso kupanga ma business osiyanasiyana uku kumakhala kufuna tendele wasosowa dzawo koma anthu ena Amanena kuti munthu kuchita bwino zimakhala zakutundu km waineo ndikuti ndizabodxa coz kwatu kwaineo kunalibe or moxi anachitako bwino km uwu umakha daliso ochokela kwamulungu bs ndiposo mukhale ndichikhulupililo chakuti mulungu akalodza kuti uyu achite bwino zimachitika bs or adani ako atachita kudumba Malele km kuchita bwino kumakha kwakufikila bs ndie plz ikani chikuluphililo chanu mwa mulungu nthawi ndinyengo idxakwana..
Day ina nditakhala padeni ndikuonera TV ndinangolandila fon km akayimbayu anali dzanga amene ndinachedza nawo dzaka zambuyomu ine nditanga fon choyamba kuyakhula dzangayi anati kod anse ulipo kod ungandilole kuti tikumane ..... ine poti uyu adali dxanga ndidamuuza eya vuto palibe umaganidza ubwera liti pondiyankha anangoti mawa kod atabwera anandiudza zotani tiye tikumane mu next part inawo pls like the page kuti tipitilize bwino thanks guys πŸ‘πŸ‘πŸ‘πŸ‘πŸ‘

24/09/2022

Yao GHETTO in fireπŸ”₯πŸ”₯πŸ”₯πŸ”₯πŸ”₯

20/09/2022

Munthu kumakharako ndidzakoπŸ™ŒπŸ™ŒπŸ™ŒπŸ”₯πŸ”₯πŸ”₯

16/07/2022

Love ur boyfriend pls don't hear for no sense

Want your school to be the top-listed School/college in Johannesburg?

Click here to claim your Sponsored Listing.

Location

Telephone

Website

Address


Dverias
Johannesburg
PUBLICFIGURE