01/10/2026
Victor Grandson Chikwi Jnr write π ππ
Azimayi dzukani!
Azimayi ambiri amangokhala.
Kukhala kwake kopanda chiyembekezo, kumangodalira support ya amunawo.
Sikuti nzolakwika kudalira mwamuna ayi koma if your husband zamuvuta kapena mwavutana, apapa mpomwe mumadziwano kuti kudalira mwamuna pa chilichonse is undesirable!
Women wake up!
Mwatengana nonse muli ndi MSCE nde mukumuona mwamuna wanu akupanga za school kuvaya college inu muli duu pakhomo.
Wakatenga diploma inu mkumuombera mβmanja.
Wakatenga degree Inu muli phee pakhomo.
Pano wavaya kunja akamabwerako akhala ali ndi masters degree koma inu simukututumuka.
Akangomaliza maphunziro akewo chikondi chikhalapo inde koma level yakanvesedwe ka zinthu isintha.
Mwamunatu akamamusiya mkazi kuti ndosaphunzira nkhani imakhala UNDERSTANDING OF THINGS IN THE CONTEMPORARY WORLD!
Amakusiyani chifukwa you fail to understand basic things nde amaona ngati pali gap.
As heβs doing school inunso go!
Ngati simungakwanitse kupita ku college learn these two things formally:
1. Baking
2. Hair Styling
Mkazi akangoziwa zinthu ziwiri izizi amakhala dolo.
Ine simnaonepo mkazi odziwa baking akungokhala kukhala kuti kukhala basi.
Ine simnaonepo mkazi odziwa za salon akungokhala opanda chiyembekezo.
Iwe zoona kukanika kupita pa technical kukaphunzira tailoring uli duu pomwe mwamuna wako ali ku Mzuni upgrading his skills.
Iwe kukanika kuphunzira kanthu kenakake koti mwamuna wakoyo akhoza kumauza anzake kuti mumatha.
Banjatu sikuchapilana.
Banjatu sikuphikilana.
Banja sikutchulana hane, dale sweet and babe ayi.
Banjatu ukalitengera chibwana limabwata ngati kalongonda ophikira mtengo wa pine.
Banja sikubanjana kokhatu banja limafuna kupangana support.
How can you support your man if you are unsupported file?
Go out and learn something that can make you make money and marketable.
Takaphunzireni kupanga sausage.
Think, take an action then repeat.
Birthday ya amunako mβmalo mowapanga surprise ndi special cake ukuwapemphanso ndalama amunako omweo yoti ukagulire cake birthday yokhala yawo, pali nzeru?
Ine nde sindingapereke ndalama imeneyo kulibwino ndibwelerane ndi Vanessa, ndi wamwano inde koma amatha kubeka.
God bless your hustle.
Inu tabwerani muphunzire za baking komaso zithu zina
Monga
Cake
Ice cream
Yorgut making
Nyamakhobwe
Swan freezers
Date pa 12 October up to 14 October
Fees ndi 5000
Register now 0986795267