24/07/2024
Malo ano ndipamrne timayankha mafuso okhudza mabanja komaso zimbwezi za chiyembekezo maka kwa achinyama,chomcho ngati mukukumana ndi mavuto amtundu uliwonse pa banjapo,bwerani tiwuzeni ndipo pano muthandizidwa ndipo mukhalaso pa banja labwino,ubwezi wabwino,kuthetsa banja si solution yothana ndi vuto mukukumana nalo,dziwani kuti vuto ndi mtimaaaaa!ndiye pano pali malangizo abwino,inu tulani nkhawa zanu basi