Evangelist Elder Ronald Ronnie Lamba

Evangelist Elder Ronald Ronnie Lamba JESUS IS COMING SOON

MKANGANO WA UKULU(The Great Controversy)Kotale uyuyu...mmmmm muli minofu abareπŸƒπŸƒπŸƒπŸƒ
30/05/2024

MKANGANO WA UKULU(The Great Controversy)

Kotale uyuyu...mmmmm muli minofu abare

πŸƒπŸƒπŸƒπŸƒ

CHIBVU 3:9Taona,ndikupatsa ena oturuka m'sunagoge wa satana akudzinenera okha ali Ayuda,osakhala Ayuda,komatu anama;taon...
10/04/2023

CHIBVU 3:9

Taona,ndikupatsa ena oturuka m'sunagoge wa satana akudzinenera okha ali Ayuda,osakhala Ayuda,komatu anama;taona ,ndidzawadzetsa alambire pa mapazi ako,nazindikire kt ine ndakukonda,

Alipo ena amazitcha akhristu asali akhristu,kuziyenereza pa maso pa a anthu ngati opemphera,otumikira,ma prophet,abusa km pa maso pa Mulungu ali osakwanira,tikuyenera zi ntchito zathu zikhale zofanana monga ife otumikira ake..Amen.

Iyi ndiye link ya group yi pa wtsp or +27738756109,Amen.
03/04/2023

Iyi ndiye link ya group yi pa wtsp or +27738756109,Amen.

WhatsApp Group Invite

OWERENGA KHALA MASO
08/01/2023

OWERENGA KHALA MASO

Kutengera ndi momwe ndimalimvera Bible maka pa Exodus 20:4,5..ndidapeza kt Yehova Mulungu,mwana komanso mzimu oyera mu u...
20/12/2022

Kutengera ndi momwe ndimalimvera Bible maka pa Exodus 20:4,5..ndidapeza kt Yehova Mulungu,mwana komanso mzimu oyera mu utatu mu umwini wake,sitikuyenera kumamupembeza kudzera mu zojambura,ziboliboli km kudzera mu mau bc,inunso mumamva momwemo,nanga cfkwa ciani muli ndi ziboliboli ma nyumba,ma office,ma church,mu khosi mwanu,mu galimoto yanu,zofananiza Mu Umulungu utatu ngati mukuzilambira ndi kuzikhulupilira ngati Yehova Mulungu,Mwana ngakhalenso mzimu oyera,kd mukatero simumakhala mukulambira Fano?

Moni ana  a Mulungu konse komwe tili?
09/11/2022

Moni ana a Mulungu konse komwe tili?

Moni ana apa ulendo?
09/11/2022

Moni ana apa ulendo?

Marko 16:16Kd mau oti "UBATIZO"amatanthauzanji,nanga inu muli ndi kuonjerapo motani pa zomwe mumaziziwa pa mau amewa?.
11/10/2022

Marko 16:16

Kd mau oti "UBATIZO"amatanthauzanji,nanga inu muli ndi kuonjerapo motani pa zomwe mumaziziwa pa mau amewa?.

25/07/2022

YOBU 2:10, kt tilimvetse ofunika kuyambira pa mdime 1 ya chapter cimeneci ca Yobu 2, inu mwaphunzirapo zotani?

30/06/2022

Pangani like page yanga, kt mudalitsike ndi mau a Muliko kudzera mu buku lake lotchedwa BAIBULO, kulimbikisana za cisautso cikudzaci, mdzukiro, kuziwa za mu nthawi yomwe tili potengera (Daniel chapter 2 komanso Revelation 14:6) ndi Jerusalem watsopano.Tiyeni tikhale limodzi, musandisiye ndekha, Amen!!

Address

Blantyre, Malawi
Benoni

Telephone

+27738756109

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Evangelist Elder Ronald Ronnie Lamba posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share