26/05/2022
A ram has been sentenced to 3 years in prison for
headbutting a woman to death in South Sudan.
The Police said they arrested the ram instead of the
owner because the owner is innocent.
The ram will belong to the victim's family after it
serves its jail sentence.
Reported by lawrence sarab elias
26/05/2022
The European Council President Charles Michel visited
Kyiv, Ukraine today as he discussed sanctions against
Russia, defense and financial support to Ukraine and
answers to a survey on compliance with EU criteria.
In a joint press briefing with the EU leader, Ukraine
President Volodymyr Zelensky, said Ukraine and the
European Union will cooperate closely to investigate
Russia's war crimes on Ukraine.
"We really appreciate the personal support of Charles
Michel and the EU help, good, truth and justice will
surely prevail," Zelensky said.
He further thanked Michel for what he called meaningful
meeting and solidarity with the people of Ukraine.
Zelensky then urged those with weapons and
ammunition to provide them to his country as it is what
they need most.
"It's not fair that Ukraine is still forced to ask about
what partners have been stored somewhere in
warehouses for years, if they have the weapons Ukraine
needs here and now, if they have the ammunition we
need here and now, it is their first moral duty to help
protect freedom, to help save lives of thousands of
Ukrainians," Zelensky said.
30/04/2022
KALIKONSE TIKAONA MU 2022.
CHILUNGAMO PARTY
21/04/2022
FIRST LIKE OUR PAGE

Reported by lawrence sarab elias.
11/04/2022
ZINA ZOKHUDZANA NDI MAIKO A RUSSIA NDI
UKRAINE.
Maiko a Russia ndi Ukraine anali Mamembala a Bungwe
la Mgwilizano wa Maiko otchedwa kuti Soviet Union,
ndipo mu Mgwilizano umenewo munali Maiko Khumi ndi
Asanu (15).
Ndipo Bungwe la Mgwilizano wa Maiko, otchedwa kuti
Soviet Union, unakhazikitsidwa Mchaka cha 1922 ndipo
Bungwe Limenelo Linatha Mchaka cha 1991.
Pa nthawi ya Mgwilizano umenewo, Dziko la Russia
Linkadzitenga kukhala Mtsogoleri wa Bungwelo ndipo
kuti Maiko omwe anali Mamembala a Bungwelo anali
mkwapa mwa Dziko la Russia.
Bungwelo Litatha, Maiko ena omwe anali Mamembala a
Soviet Union, anaganiza zolowa Bungwe la Mgwilizano
wa Maiko otchedwa NATO, koma izi sizinasangalatse
Dziko la Russia.
Ndipo kwa nthawi yaitali, Mgwilizano wa NATO,
unakhala ukuyesetsa kuti ugwire ntchito limodzi ndi
Dziko la Russia, koma izi zinakanika mpaka Mchaka cha
2014.
Dziko la Russia, Linalanda Chigawo chotchedwa Crimea
M'dziko la Ukraine ndipo Bungwe la NATO,
Linakanitsitsa kuvomeleza kuti Chigawocho ndi Mbali
imodzi ya Dziko la Russia.
M'mwezi wa November, Mchaka cha 2018, Asilikali a
Dziko la Russia, anakalanda Sitima ya M'madzi ndi
kusunga mwachikakamizo Anamalinyelo a Sitimayo
yomwe inali M'nyanja yotchedwa Azov, M'dziko la
Ukraine ndipo Dziko la Russia Linapitiliza pokamanga
Mlatho pa nthaka ya Dziko la Ukraine.
M'mwezi wa April, Mchaka cha 2019, Nduna zowona
zakunja kwa Maiko a Mgwirizano wa NATO,
anagwilizana zokhazikitsa Dongosolo Lothandiza Dziko
la Ukraine pa zomwe Dziko la Russia Linkachita.
Ndipo M'mwezi wa April, Mchaka cha 2021, Dziko la
Russia, Linayamba kutumiza Asilikali ake kukazungulira
Dziko la Ukraine ndipo Dziko la Russia Linakanitsitsa
kuti Linali ndicholinga chofuna kulanda Dziko la Ukraine.
Bungwe Lotchedwa NATO, Liri ndi Maiko okwana
Makumi atatu (30) omwe ndi Mamembala ake ndipo
palibe umboni okwanira oti Dziko la Russia
Lingagonjetse Mgwilizano umenewu.
Pomaliza osaiwala kupanga like page ino komanso mutipeza pa whatsapp # iyi
0888523104.
10/04/2022
UTHENGA WA PADERA
Tikudziwitsa anthu onse amene amasatira page ino kuti takhazikitsa group pa whatsapp.
Cholinga cha group imeneyi ndi kukupasirani magawo awa;
>Nkhani za kunja komanso kwathu kuno kuphatikizirapo nkhondo ya russia komanso ukraine.
>Ma vacancies
Kuti tikupangeni add group imeneyi mukuyenera kupanga like page ino and pitani ku inbox yanga pa # iyi 0888523104 kuti tikupangeni add osati muike # yanu.
Sarab online
Send a message to learn more
01/04/2022
NKHANI ZOKHUDZANA NDI NKHONDO YOMWE
IKUCHITIKA M'DZIKO LA UKRAINE.
Lero pa 1st April, Ndi Tsiku la Nambala 37 kuchokera pa
24th February pomwe Nkhondo inayambika M'dziko la
Ukraine.
Ndipo Lero, Nthumwi za Maiko a Russia ndi Ukraine ndi
Ukraine zikuyembekezeka kupitiliza zokambirana zawo.
Koma Unduna wa Zachitetezo M'dziko la Britain, wati
Dziko la Russia Likukhazikitsa Asilikali ake M'dziko la
Georgia ndicholinga choti adzichokera kumeneko
ndikumakanyenya Nkhondo M'dziko la Ukraine.
Dziko la Ukraine, Latsimikiza kuti Asilikali a Dziko la
Russia omwe analanda Malo opanga Mphamvu za
Magetsi otchedwa Chernobyl power Plant, achoka pa
Malopo.
Komanso Asilikali ena a Dziko la Russia omwe anali
Ntauni yotchedwa Slavutych nawonso achoka Ntauni
imeneyo.
Dziko la Ukraine, Latsekula Milandu yokhudza Asilikali a
Dziko la Russia, yokwana 3,457, Ndipo izi zachitika,
Dziko la Ukraine Litafotokoza kuti Ana okwana 148
ndiomwe anaphedwa ndi Asilikali a Dziko la Russia.
Ndipo Dziko la Ukraine, Latsitsa Maudindo a
Mbalamatodya ziwiri za Asilikali a Dzikolo omwe anali
ndi Udindo wa General.
Ndege ziwiri za Nkhondo za Dziko la Ukraine zaphulitsa
Mabomba pa Malo awiri osungira Mafuta a Galimoto,
M'dziko la Russia, Wafotokoza izi ndi Bambo
Vyacheslav Gladkov yemwe ndi Bwanankubwa wa
Mzindawo.
Ndipo kameneka ndikoyamba kuti Asilikali a Dziko la
Ukraine akalowe ndi kuphulitsa Mabomba M'dziko la
Russia.
Mtsogoleri wa Dziko la Russia, Bambo Vladimir Putin
wati Dziko lake Lipitiliza kugulitsa M'mpweya wa Gasi
ku Maiko aku Ulaya ngati Maikowo atavomeleza polipira
Ndalama ya Rouble yomwe ndi Ndalama za Dziko la
Russia.
Izitu ndiye nkhani zokhudza ndi Nkhondo yomwe
ikuchitika M'dziko la Ukraine M'mawa uno ndipo pano
pa SARAB ONLINE tikhala Tikutsatira bwino zonse zokhudza
Nkhondo imeneyi zokambirana za Maiko a Russia ndi
Ukraine.
Komanso inu pindani Manja anu ngati M'mwenye
Msitolo podikira kuti Tifotokoze zomwe zikuchitika pa dziko la pansi.
18/03/2022
FIRST LIKE PAGE
ZINA ZOKHUDZANA NDI MAIKO A RUSSIA NDI
UKRAINE.
Maiko a Russia ndi Ukraine anali Mamembala a Bungwe
la Mgwilizano wa Maiko otchedwa kuti Soviet Union,
ndipo mu Mgwilizano umenewo munali Maiko Khumi ndi
Asanu (15).
Ndipo Bungwe la Mgwilizano wa Maiko, otchedwa kuti
Soviet Union, unakhazikitsidwa Mchaka cha 1922 ndipo
Bungwe Limenelo Linatha Mchaka cha 1991.
Pa nthawi ya Mgwilizano umenewo, Dziko la Russia
Linkadzitenga kukhala Mtsogoleri wa Bungwelo ndipo
kuti Maiko omwe anali Mamembala a Bungwelo anali
mkwapa mwa Dziko la Russia.
Bungwelo Litatha, Maiko ena omwe anali Mamembala a
Soviet Union, anaganiza zolowa Bungwe la Mgwilizano
wa Maiko otchedwa NATO, koma izi sizinasangalatse
Dziko la Russia.
Ndipo kwa nthawi yaitali, Mgwilizano wa NATO,
unakhala ukuyesetsa kuti ugwire ntchito limodzi ndi
Dziko la Russia, koma izi zinakanika mpaka Mchaka cha
2014.
Dziko la Russia, Linalanda Chigawo chotchedwa Crimea
M'dziko la Ukraine ndipo Bungwe la NATO,
Linakanitsitsa kuvomeleza kuti Chigawocho ndi Mbali
imodzi ya Dziko la Russia.
M'mwezi wa November, Mchaka cha 2018, Asilikali a
Dziko la Russia, anakalanda Sitima ya M'madzi ndi
kusunga mwachikakamizo Anamalinyelo a Sitimayo
yomwe inali M'nyanja yotchedwa Azov, M'dziko la
Ukraine ndipo Dziko la Russia Linapitiliza pokamanga
Mlatho pa nthaka ya Dziko la Ukraine.
M'mwezi wa April, Mchaka cha 2019, Nduna zowona
zakunja kwa Maiko a Mgwirizano wa NATO,
anagwilizana zokhazikitsa Dongosolo Lothandiza Dziko
la Ukraine pa zomwe Dziko la Russia Linkachita.
Ndipo M'mwezi wa April, Mchaka cha 2021, Dziko la
Russia, Linayamba kutumiza Asilikali ake kukazungulira
Dziko la Ukraine ndipo Dziko la Russia Linakanitsitsa
kuti Linali ndicholinga chofuna kulanda Dziko la Ukraine.
Bungwe Lotchedwa NATO, Liri ndi Maiko okwana
Makumi atatu (30) omwe ndi Mamembala ake ndipo
palibe umboni okwanira oti Dziko la Russia
Lingagonjetse Mgwilizano umenewu.
Kodi ngati Dziko la Russia Latha Masiku oposa Makumi
awiri (20) Likulimbana ndi Dziko.
16/03/2022
FIRST LIKE PAGE
Despite all the destruction happening in Ukraine after
Russia's invasion Ukrainian President Volodymyr
Zelensky remains confident that the country will be
strong again.
On Monday,more than 4,000 people left the besieged
city of Mariupol with more evacuation efforts planned
today as powerful explosions rock the Ukrainian capital
Kyiv with Russian air strikes hit residential buildings and
a metro station.
"We will restore everything, every street of every city,
every house, every apartment and we will direct all our
efforts to this, all the help of the world and we are
already forming funds for Ukraine to live," President
Zelensky said.
Almost all of the Russian military advances remain
stalled despite heavy bombing, says a senior US defence
official and a journalist has reportedly been arrested
after interrupting Russian state TV with a sign reading
"no war".
The EU unveils more sanctions against Russia, targeting
luxury goods exports as well as investments in its
energy sector.
06/03/2022
CHITHU CHOOPSA CHICHITIKA PA DZIKO LONSE LAPANSI.
Posachedwapa tikupasilani satanesatane pa zomwe zikufuna kuchitika pa dziko lonse la pansi.
Pangani like page ino and share kwa azanu kuti nawo amve nawo nkhani.
04/03/2022
RUSSIA YATULUTSA SITIMA YAKE YOOPSA KWAMBIRI
YOTCHEDWA 'TYPHOON'
Sitima yoopsa kwambiri padziko lonse yotchedwa
'Submarine Typhoon' yatulutsidwa.
Sitimayi ndiya dziko la Russia ndipo mwa zina ili
ndikuthekera komila m'madzi ndikuyenda pansi pa
nyanja kwa masiku 120.
Sitimayi ndiyayitali ma metre 175 ndipo imasungila ma
bomba 24 amphavu kwambiri oti akhoza kuononga
theka la Europe mu mphindi zochepa.
Anthu ogwila ntchito okwanila 160 ndi omwe
amafunikila kuti Sitimayi igwile ntchito yake pa Madzi.
Sitimayi yakhala ikusungidwa ku 'Reserve' kwa nthawi
yayitali koma yatulutsidwa pa nthawi yomwe Russia
ikulimbana ndi Ukraine.
03/03/2022
KODI MUKUDZIWA?
TSATANETSATANE WA MKANGANO WA PAKATI PA
RUSSIA NDI UKRAINE
choyamba, tikuyenera kudziwa kuti dziko la Russia
komanso Ukraine ndipachibale(ndamodzi), maiko
awiriwa adali ophatikizana ndipo amkalamuliridwa ndi
boma limodzi. panthawiyo maiko onsewa adali mu dziko
limodzi lotchedwa kuti Soviet Union.
Soviet Union imkapangidwa ndi maiko 15, maikowa ndi
Russia, Ukraine, Georgia, Belorussia, Uzbekistan,
Armenia, Azerbaijan, Kazakhstan, Kyrgyzstan, Moldova,
Turkmenistan, Tajikistan, Latvia, Lithuania komanso
Estonia. likulu (capital city) la maikowa lidali Moscow
yomwe pano ndi capital city ya Russia.
mu chaka cha 1991, kutsatira ndi kugwa kwa boma la
mu nthawiyo, dziko lotchedwa Soviet Union
lidaphwasuka ndipo maiko 15 onsewa adapatukana
mkukhala maiko oima paokha. potengera kuti Army
yawo idali imodzi, maikowa adangogawana asilikali
komanso zida, koma dziko la Russia ndilomwe lidatenga
gawo lalikulu la chuma cha Soviet Union. potengera kuti
maikowa adali dziko limodzi, dziko la Russia limakula
kwambiri mphanvu pa ndale komanso chitetezo cha
maikowa.
√>>tisanapitilire, titsekulane kaye mitu.
itatha World War 2, maiko akuluakulu amaika kwambiri
masomphenya pa chitetezo, kotero kuti akhala
akupanga zida zoopsa, komanso maiko omwe
sagwirizanawa omwe ndi ma super power safuna
aziyandikirana. America siingalore kuti iyandikane ndi
Russia kapena China mwanjira ina iliyonse,
chimodzimodzinso Russia.
mkangano wa maiko awiriwa udayambika mu chaka
cha 2014. mu chaka cha 2014 mu mwezi wa February,
mu dziko la Ukrain mudabuka zionetsero za ndiwe yani,
anthu ochita zionetsero adagwetsa boma la munthawiyo
ndipo president *Viktor Yanukovych* adamuchotsa pa
mpando, president yu amkagwirizana kwambiri ndipo
anali pa ubwenzi wabwino ndi dziko la Russia. mu
nthawi ya zionetseroyi, anthu osachepera 100
adaphedwa. kumanenedwa kuti maiko akumadzulo kwa
Europe komanso America ndamene adachititsa izi
pofuna kugwetsa boma lomwe limkagwirizana ndi dziko
la Russia lo.
kutsatira ndi
02/03/2022
BREAKING NEWS: MAWUNTHENGA OMWE MAYIKO
ANZUNGU NDI ENA AMUNO MU AFRICA MONGA
MALAWI AMATULUSA POWOPHYEZA DZIKO LA RUSSIA
ASIYA DZIKO LONSE LAPANSI PAMOTO
Dziko la Russia lawuza mayiko onse omwe ali pansi pa
NATO, United Nations kuphatikizapo mayiko ena 4
amuno mu Africa omwe ndi Malawi, South Africa, Kenya
ndi Nigeria kuti iye samaseka ndizigawenga zomwe
zikufuna kuwononga dziko lake kotelo nthawi ina
iliyonse akhala akutumiza maboma omwe atekese
ndikuwononga nthaka kumayiko omwe akunyoza
kapena kunyogodola dziko lake.
Posonyeza kukwiya kwake dziko la Russia latchela
mabomba ake a Nuclear omwe samathekeka
kuphelesedwa pogwilisa ntchito network yamtundu wina
uliwonse ndipo ali ndikuthekela kopha chamoyo china
chilichonse kupatulako dziko la Russia ndi amene
angakhale kutali ndikomwe kungagwele bombalo.
Izi zikutanthawuza kuti bomba la Satan 2 litha kulowa
ndikuphulisa dziko la USA lomwe limadalila kwambili ma
satellite ndi network pophelesela mabomba
Asilikari a adziko la Russia otchedwa Chencheni omwe
anatumidwa ndi mtsogoleri wa dzikolo kuti akaphe
mtsogoleri wadziko la Ukraine onse aphedwa.
Pakanali pano Putin wawuza asilikari ake ankhondo kuti
agwilise ntchito njira ina iliyonse yoophya kupha
mtsogoleri wadziko la Ukraine pomunena kuti
ndichigawenga ndipo mabomba otchedwa Satan 2
ayamba kale kulila kuti ng'wiiiii kudikila bwana alamule
ndikulilondolela kogwela
Mukawona muchithuzimo Russia ndidziko lowophya
kwambili lili pa number 1 padziko lonse lapansi
ngakhaleso China yomwe ili pambuyo pake nayo
ndiyowophya ili pa number 3
01/03/2022
koma tisayiwale kuti Covid-19 inakalipo ndipo sinathe.
Zili ndi inu ndi ine kutsatira ndondomeko zonse
zopewera nthendayi.
Imodzi mwa njira zopewera nthendayi ndiyo kubaitsa
katemera kuti inu ndi okondedwa anu musakhale
pachiopsezo.
Kodi mukudziwa kuti katemera wa AstraZeneca
wayambaso kupezeka m'dziko muno tsopano???
Kwa ife tonse omwe timadikira katemera wathu
wachiwiri wa AstraZeneca, nthawi yoyenera ndi
imeneyi...
More
01/03/2022
The International Criminal Court's prosecutor says he
wants to investigate Russia for possible war crimes as
up to 70 Ukrainian soldiers have been killed in a
Russian artillery strike on the north-eastern city of
Okhtyrka.
This follows a huge convoy of Russian armour, about
40 miles long advancing on Ukraine's capital Kyiv.
According to local journalists in Kherson say the
regional centre is almost completely surrounded by
Russian troops.
Negotiators for Kyiv and Moscow have held talks in...
More