Jimmy Janleck Sephass

Jimmy Janleck Sephass

Share

03/04/2025

Foolish fools 😎

21/10/2023

Salute to He who lives forever.
I love💕 you Jesus

15/05/2023

Because He lives

25/04/2023

When the hunter is hunted 😁 and the predator becames a prey

03/05/2022

*Timangoonana anthufe koma background yathu enafe ndiyomvetsa chisoni😢*

*Takolapo mbalame ndi ulimbo komanso kutcherapo mbalame za mzisa ndi matchera🥲*

*Tavinapo mganda komanso kupitako kunyau ndi kukazuzidwa🥲*

*Takhalapo pakhomo lanyumba la Kwa achibale komanso kwa neba kudikirira Kuti atiyitanire chakudya uku tikukhosomora kachifuwa kowadziwitsa Kuti tili pakhonde pa nyumba yawo, pena timaitanidwa pena ayi🥲*

*Tinkayenda mtunda wapansi wopita Kusukulu, chimanga chokazinga chili m'botolo, kakope ndi pensulo zodula zili mu m'pepala la sugar, kamphepo kozizira kochokera mu mchigwa cha mchiguluwindi, kakuomba molapitsa kumanso popeza zovala zodzitetezera ku mphepo sitinkazidziwa🥲*

*Zovala nazo zinali zomwezomwezo, zomwe zimavalidwa lolemba mpaka lachisanu. Kuphanzi tikuyenda chiwetochiweto ndipo kutafika pochita chikanamba kamba kosavala nsapato komanso kosamba chinyenga mphunzitsi🥲*

*Nthawi ya break ku sukulu nako, kutoleza zakudya zomwe ena egwetsa monga chimanga chokazinga, chidali chizolowezi chathu🥲*

*Pobwerera kunyumba timayesa kusenda kasamvu kamtengo wina wake tiganiza Kuti tikapeza nsima kunyumba ndiwo ndi nyama, koma tsoka ilo pena timakapeza kuti kulibe popeza ufanso umakhala kuti kulibenso🥲*

*Ukagwira maganyu olima Kuti tipeze zosowa zathu chidali chizolowezi chathu🥲*
*adatipanapo ndi chitseko ife posuzumira mnyumba mwa eni kuti tionereko TV ya black and white.*

*Tinkakoza pogona ife ndikuchitanso mwano osayanika ka gombeza kathu kong'ambikako ndipo timavutika mazulo pogona*

*Mutamationa kulimbikiraku n'kufuna kuti tisinthe nyengo zathu ndikuti ana athu asadzavutikenso ngati mmene ife tinavutikira🙌🙌*

*mulungu amakonda aliyense ndipo ndi wokhulupirika tisamachedwe n'kulira, dzukani ndipo tiziyendebe mpaka titapeza

25/12/2021

Merry Xmas to y'all family n friends. Love you

15/12/2021

Believing is seeing

24/10/2021

May we all have a restful sunday

14/04/2021

Jesus, the master of the game🙏🙏

17/03/2021

Missing the target😎

22/02/2021

The other side of life is our destination

21/02/2021

Teach me teacher!

Want your school to be the top-listed School/college in Zomba?

Click here to claim your Sponsored Listing.

Location

Category

Telephone

Website

Address


Jsephass@gmail. Com
Zomba