Iyiyi ndiya pa Chanco

Iyiyi ndiya pa Chanco The university that God loves the most in short the forth arm of Malawi governments Chanco

Kodi munthu akamuwida timamufunsa bwanji? Zikundivuta ine kuti ndifunsa bwanii 😅
16/09/2026

Kodi munthu akamuwida timamufunsa bwanji?
Zikundivuta ine kuti ndifunsa bwanii 😅

The legendary MDU macheza ako timawasowabe.Keep resting in peace GOAT.
09/09/2026

The legendary MDU macheza ako timawasowabe.
Keep resting in peace GOAT.

Koma week end’yi ziwalo ndikuzimvera chisoni 😅
03/09/2026

Koma week end’yi ziwalo ndikuzimvera chisoni 😅

Akulu awa kodi ayamba kale kupanga campaign? 😅Let’s be serious guys momoti muyambe kaye kupanga za fees must fall mukuli...
02/09/2026

Akulu awa kodi ayamba kale kupanga campaign? 😅
Let’s be serious guys momoti muyambe kaye kupanga za fees must fall mukulimbana ndi izi?

Graduation imaoneka yophweka akakhara akupanga ndanzako
23/08/2026

Graduation imaoneka yophweka akakhara akupanga ndanzako

Ngati mukukaniza ma gown wo mukanangotiuza nanga chi process chake chimenechi?The number one University you can do bette...
17/08/2026

Ngati mukukaniza ma gown wo mukanangotiuza nanga chi process chake chimenechi?
The number one University you can do better ndithu 🥱

Kukamwa kuli yasa kodi ndichani chimenechi?Palibe mkazi wapa Unima anaonako izi
23/07/2026

Kukamwa kuli yasa kodi ndichani chimenechi?
Palibe mkazi wapa Unima anaonako izi

Pali zinthu zina sumafunika kuti munthu uvomele olo zitavuta chotani maka izizi zama social media zimasokoneza brand.Any...
23/07/2026

Pali zinthu zina sumafunika kuti munthu uvomele olo zitavuta chotani maka izizi zama social media zimasokoneza brand.

Anyway ife izi simbali yathu timafuna tingogawanako nkhani zomwe zikuchitika pakati pama graduate ama University enawa

Kodi atsikana nokhanokha mumadyana choncho eti eeh zowopsatu
23/07/2026

Kodi atsikana nokhanokha mumadyana choncho eti eeh zowopsatu

Apa nde sizinayendetu MHSRIP 💔🥲
20/07/2026

Apa nde sizinayendetu MHSRIP 💔🥲

Address

Chilunga
Zomba

Opening Hours

Saturday 07:30 - 16:30
Sunday 09:00 - 17:00

Telephone

+265883931881

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Iyiyi ndiya pa Chanco posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share