Iyi si sukulu wambatu akakufunsani za sukulu yabwino ya chisilamu awuzeni kuti yapezeka aponyeleni ka picture aka timvane nawo ku inbox
A SCHOOL THAT GIVE ISLAMIC AND SECULAR EDUCATION
Operating as usual
Iyi si sukulu wambatu akakufunsani za sukulu yabwino ya chisilamu awuzeni kuti yapezeka aponyeleni ka picture aka timvane nawo ku inbox
iyi ndi sukulu yomwe ikupeleke maphunziro a chizungu ndi a chisilamu pa mtengo wosaboola mthumba ndipo fees mmapeleka pang'ono pang'ono fees kwa atsikana ku primary ndi 80,000 pomwe ku secondary ndi 120, 000. Kwa anyamata 60,000
Ya anyamata ili ku machinga pa boma penipeni ya atsikana ili ku zomba ku songani