Lospa and Spiz comedy

Lospa and Spiz comedy It's all fun and music promoter

27/11/2024

Ndalanda mkaz wa baunsa .ndtani gyz akut akufuna andpezeπŸ€”πŸ€”πŸ€”πŸ€”πŸ€”πŸ€”πŸ€”

24/11/2024

Sindkuziwa chifkwa chmene aphuzisi andmenyera.andfusa bwinobwino kt nkhuku ya ikaz mchizungu nchan???
Ndawayankha female chicken/female meat ndangodabwa mbamva abale kaya ndalakwanji kaya😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭

21/11/2024

Kod nkhani za uku ndi uku anasiya?

04/11/2024

Sitingakwatire pano Zaka 36 zachepaπŸ˜€πŸ˜€πŸ˜€

21/10/2024

Kuli Mwai wa ntchito Kuno mkaipeza nafeso tiithamangire

29/10/2023

Amene anayambisa masamu ankamuchonga ndani ndipo ma answers ochongayo amawatenga kuti?πŸ˜€πŸ˜€πŸ˜€πŸ˜€πŸ˜€80marks

25/10/2023

Pamene mzanu anasiila school ndpomwe anamalizila kaya anasiila STD 6 ndpomwe iyeyo anamalizila tisamasekane

23/10/2023

Ntchulani ma artist awiri omwe atulusa ma album opanda hit song ndipo muwapase langizo limozπŸ€₯πŸ€₯πŸ€₯πŸ€₯πŸ€₯πŸ€₯

23/10/2023

Vuto mmazimva kt inuo simchimwa ukakhala muuchimo umakhala blinds suzwaso zoti ukuchimwaπŸ˜€πŸ˜€πŸ˜€πŸ˜€πŸ˜€

22/10/2023

Why jay jay cee kutulusa nyimbo 26 km no hit song fame nd nthawi.other people says asinthe style akuimba ya chikale but achina gattah amaimba old hip hop km amavekabe😫😫😫😫😫😫😫

21/10/2023

Ndi forest iti yomwe yosefe ankatengako matabwa ?amene atayenkhe alandira credit
Lospa and Spiz comedy

20/10/2023

Si nose anakulengani kuti mzakwatiwa .kod bachala wa mkazi mchizungu nchaniπŸ˜›πŸ˜œπŸ˜œπŸ˜œ

Address

Zomba

Telephone

+265998692316

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Lospa and Spiz comedy posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The School

Send a message to Lospa and Spiz comedy:

Shortcuts

Share