
Mphunzitsi wa Chingerezi
This page is created to help directing those people who either have never been to school or have bee
Operating as usual

Sukulu yophunzitsa Chingerezi ya pa Whatsapp yochedwa Learning English language online ikupitirirabe. Anthu akupindula ndi sukuluyi moti ena akuyamikira ndithu.
Kaya simudziwa Chingerezi koma mukufuna mutadziwa, kaya mumaidziwa pang'ono mufuna mutapitiriza kudziwa kuyankhula Chingerezi, kaya mumadziwa koma mumalephera kulumikiza mawu nkumayankhula, ena mumangomva Chingerezi koma kuchiyankhula kumakuvutani, LIPIRANI MULOWE NAWO SUKULU YOPHUNZIRA CHINGEREZI PA WHATSAPP.
Fees ndi K3,000 pamwezi, maphunziro amakhalapo kuyambira Lolemba mpaka Lachisanu kupatula weekend komanso masiku a Holiday.
Yankhulani ndi Mphunzitsi wa Chingerezi pa Whatsapp osati kuimba foni ayi, Whatsapp yokha pa 0996 111 103 potumiza uthenga wokuti, "Learning English language online."
Click here to claim your Sponsored Listing.
Location
Category
Contact the school
Telephone
Website
Address
Opening Hours
Monday | 07:30 - 20:00 |
Tuesday | 07:30 - 20:00 |
Wednesday | 07:30 - 20:00 |
Thursday | 07:30 - 20:00 |
Friday | 07:30 - 20:00 |