NVK

NVK Mediam

09/01/2026




Bwalo la Supreme ku Blantyre lakana kumva pempho la mlembi wamkulu wa chipani cha MCP a Richard Chimwendo Banda, lofuna kuti asiye kusungidwa kundende podikilira mlandu oganiziradwa kufuna kupha munthu.

Oweruza Dorothy Nyakaunda wapereka chigamulochi ponena kuti pempholi lafulumira kufika ku bwalo la Supreme, chifukwa ati bwaloli limamva nkhani zimene zagamulidwa ku bwalo lalikulu.

Chigamulochi chadza mokomera mbali ya boma, imene inapempha bwalo, ati pozindikira kuti pempholi linalo ndi zolakwika.

Zateremu ndiye kuti a Chimwendo Banda akusungidwabe ku ndende podikilira siku la mlandu wawo, ndipo a Khwima Mchizi oimira a Banda, atsimikiza kuti a Chimwendo Banda akudwala.

Mchithunzimu a Khwima Mchizi

Wolemba Daniel Zimba

24/06/2024

Mongokumbusana
Tigers 2-2 Silver

27/04/2024

Nyimbo

10/03/2024

HALF TIME

CCAP 2-1 CATHOLIC
๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚

01/09/2022

NVK..nd nfana yekhayo amene
Akuyimba chamba cha
Dancehall kuchoka ku Be good alliance the best Dancehall crew

22/04/2022
04/03/2022

NVK
FROM
BE GOOD ALLIANCE
THE BEST DANCECREW

Address

Zomba

Telephone

+265992901341

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when NVK posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share