Alosi Media

Alosi Media

Share

We inform, entertain and educate. No sad moments here

11/06/2026

PREDICT AND WIN 💰 🔥

What's your prediction?
FIFA World Cup

Mexico Vs. South Africa

Photos from Alosi Media's post 10/06/2026

MR. MALAWI WAKALE WAMWALIRA 💔

Yemwe anakhalapo katswiri ponyamula zitsulo pa mpikisano wa Mr. Malawi zaka zam'mbuyomu, Tadeyo Banda, wamwalira kutsatira kuwombelana komwe kunalipo ku Johannesburg, South Africa.

Zipolowezi zidachitika pakati pa magulu osiyana, malipoti amene atipeza zikuonesa kuti anthu 12 ndamene aphedwa pa kuombelanaku💔

Tadeyo Banda anatchuka mu zaka zamma 2000, ndipo anaziwika chifukwa chonyamula zitsulo zolemera komanso martial arts.

Rest in Peace, Tadeyo 'Mr. Malawi' Banda 💔🕊️

Osaiwala kupanga follow Alosi Media kuti nkhani zambiri zisamakuphonyeni.

10/06/2026


Inuyo mukuona kuti zomwe wanena Mady P zija zingakhale zoona? Kudya azimayi 4000?🙌😂

10/06/2026

Anyamata awiriwa anamubera mzimayi wina sausage yomwe amagulisa munsika nkuilongeza mu thalauza 😀 Kenako akuyenda imodzi inagwa kuchokera mu trouser mo zomwe zinapangisa anthu kudabwa.

Basitu awagwira kuwapitisa mnyumba pamene amawapeza ndi inanso atailongeza. Zachitika ku Zambia

Osaiwala kupanga follow Alosi Media kuti nkhani zambiri zisamakuphonyeni.

09/06/2026

Aah ife timaziwa kuti mupilo muja wabisamo zinthu😂

09/06/2026


Why is she trending?🤔

09/06/2026

Ndiye kwabwera mankhwala awa! Azimayi ambiri akufunikira amenewa😎

09/06/2026

Ngozi yake yovuta kuyilongosola kwaketu😩

08/06/2026

MNYAMATA WINA WASOWA💔


Mnyamata wa zaka 16 zakubadwa yemwe amaphunzira pa sukulu ya Msalura Sekondale m'boma la Salima Justin Makosana sakupezeka chisoweleni pa 31 May chaka chino.

Malingana ndi makolo a mwanayu, Justin amayenera kulemba nawo mayeso a folomu 2 omwe ali mkati ndipo amakhala limodzi ku dera la Chimweta m'bomali.

Patsiku losowali, Justin anavala malaya a white ndi buluku la black ndipo anthu akupemphedwa kuimba phone pa 0999391203, 0995879485 kapena kukanena kupolisi yomwe muli nayo pafupi.

Follow Alosi Media for these and more!

Want your school to be the top-listed School/college in Zomba?

Click here to claim your Sponsored Listing.

Location

Telephone

Website

Address


Zomba