Fostino Bonister

  • Home
  • Fostino Bonister

Fostino Bonister I am proudly announces that I am professional photographer ,electrical installation,tailoring and primary school teacher

31/08/2026
22/03/2026

adani anu onse akusala kudya kuti mumwalira afote ndi kunyala ngati mkuyu

13/08/2025

Moyo umafuna zilikutali basitu

04/06/2023

Aliyese pamalo pake akhale

23/11/2021

Buku Lopatulika 1992 Levitiko 19:26-29 Musamadya kanthu ndi mwazi wace; musamacita nyanga, kapena kuombeza ula. Musamameta mduliro, kapena kusenga m'mphepete mwa ndebvu zanu, Musamadziceka matupi anu cifukwa ca akufa, kapena kutema mpbini; Ine ndine Yehova. Usamaipsa mwana wako wamkazi ndi kumcititsa cigololo; lingadzale ndi cigololo dzikoli, ndi kudzazidwa nazo zocititsa manyazi.

22/09/2021

Kuvomereza kumavuta makamaka ukakhala kuti wataya nthawi pa chimenecho.

1.kuvomereza kuti supedza ntchito ya my office pamene uli ndi PhD,master degree, degree, diploma,certificate and experience .ndikuyamba kulima kumudzi ,umapitilizabe kutaya kochepa komwe umapedza kupangira apply.umangoona wafika dzaka 37 .

2.kuvomereza kumavutadi ,wachikondi wako kukuudza kuti chatha koma usakuudza chomwe walakwa.

3.kuvomereza kumavuta kwambiri ,akukuudza kuti inuyo ndiwosavomeredzeka pamene wagwira ntchitoyo kwa zaka 4 popanda vuto.

4 .kumavuta kuvomereza kuti akuchosa mpingo chifukwa unalalika ulaliki womwe anthu anaukonda ndapemphanso kuti mudzaubweredzenso. Umaona ngati zonama angokuyetsa .

15/09/2021

Buku Lopatulika Yesaya 45:2-7

YEHOVA AMAYESA KUKHALA KOLESI CHIPANGIZO Ndidzakutsogolera ndi kusalaza pokakala; ndidzatyolatyola zitseko zamkuwa, ndi kudula pakati akapici acitsulo; ndipo ndidzakupatsa iwe cuma ca mumdima, ndi zolemera zobisika za m'malo am'tseri, kuti iwe udziwe kuti Ine ndine Yehova, amene ndikuitana iwe dzina lako, ndine Mulungu wa Israyeli. Ndakuitana iwe dzina lako, cifukwa ca Yakobo mtumiki wanga ndi Israyeli wosankhidwa wanga; ndakuonjezera dzina, ngakhale iwe sunandidziwa Ine. Ine ndiri Yehova, ndipo palibe winanso; popanda Ine palibe Mulungu; ndidzakumanga m'cuuno, ngakhale sunandidziwa; kuti anthu akadziwe kucokera ku maturukiro a dzuwa ndi kumadzulo, kuti palibe wina popanda Ine; Ine ndine Yehova, palibe winanso. Ine ndilenga kuyera ndi mdima, Ine ndilenga mtendere ndi coipa, Ine ndine Yehova wocita zinthu zonse zimenezi.

Address


Telephone

+265885077763

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Fostino Bonister posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The School

Send a message to Fostino Bonister:

Shortcuts

  • Want your school to be the top-listed School/college?

Share