Fostino Bonister

Fostino Bonister

Share

I am proudly announces that I am professional photographer ,electrical installation,tailoring and primary school teacher

22/03/2026

adani anu onse akusala kudya kuti mumwalira afote ndi kunyala ngati mkuyu

13/08/2025

Moyo umafuna zilikutali basitu

04/06/2023

Aliyese pamalo pake akhale

23/11/2021

Buku Lopatulika 1992 Levitiko 19:26-29 Musamadya kanthu ndi mwazi wace; musamacita nyanga, kapena kuombeza ula. Musamameta mduliro, kapena kusenga m'mphepete mwa ndebvu zanu, Musamadziceka matupi anu cifukwa ca akufa, kapena kutema mpbini; Ine ndine Yehova. Usamaipsa mwana wako wamkazi ndi kumcititsa cigololo; lingadzale ndi cigololo dzikoli, ndi kudzazidwa nazo zocititsa manyazi.

22/09/2021

Kuvomereza kumavuta makamaka ukakhala kuti wataya nthawi pa chimenecho.

1.kuvomereza kuti supedza ntchito ya my office pamene uli ndi PhD,master degree, degree, diploma,certificate and experience .ndikuyamba kulima kumudzi ,umapitilizabe kutaya kochepa komwe umapedza kupangira apply.umangoona wafika dzaka 37 .

2.kuvomereza kumavutadi ,wachikondi wako kukuudza kuti chatha koma usakuudza chomwe walakwa.

3.kuvomereza kumavuta kwambiri ,akukuudza kuti inuyo ndiwosavomeredzeka pamene wagwira ntchitoyo kwa zaka 4 popanda vuto.

4 .kumavuta kuvomereza kuti akuchosa mpingo chifukwa unalalika ulaliki womwe anthu anaukonda ndapemphanso kuti mudzaubweredzenso. Umaona ngati zonama angokuyetsa .

15/09/2021

Buku Lopatulika Yesaya 45:2-7

YEHOVA AMAYESA KUKHALA KOLESI CHIPANGIZO Ndidzakutsogolera ndi kusalaza pokakala; ndidzatyolatyola zitseko zamkuwa, ndi kudula pakati akapici acitsulo; ndipo ndidzakupatsa iwe cuma ca mumdima, ndi zolemera zobisika za m'malo am'tseri, kuti iwe udziwe kuti Ine ndine Yehova, amene ndikuitana iwe dzina lako, ndine Mulungu wa Israyeli. Ndakuitana iwe dzina lako, cifukwa ca Yakobo mtumiki wanga ndi Israyeli wosankhidwa wanga; ndakuonjezera dzina, ngakhale iwe sunandidziwa Ine. Ine ndiri Yehova, ndipo palibe winanso; popanda Ine palibe Mulungu; ndidzakumanga m'cuuno, ngakhale sunandidziwa; kuti anthu akadziwe kucokera ku maturukiro a dzuwa ndi kumadzulo, kuti palibe wina popanda Ine; Ine ndine Yehova, palibe winanso. Ine ndilenga kuyera ndi mdima, Ine ndilenga mtendere ndi coipa, Ine ndine Yehova wocita zinthu zonse zimenezi.

12/07/2021
05/07/2021

First John, 3:15 - Whosoever hateth his brother is a murderer: and ye know that no murderer hath eternal life abiding in him.

18/06/2021

Ananu mwakhala mukudandaula kuti nkhuku mumapasidwa zipalapasiro ndi phikophiko ndikukuudzani njira izi

1.zinthu zomwe amakondadzo mudzichosemo asanaphike muwaudzi kuti mudxiphikira padzokha nthawi ina.

2.bwerani ndi mulendo nzanu wakutali .

Mudzadya zachilendo ndithu.

Pangani like and share to hear more fact .

12/06/2021

Buku Lopatulika 1992 1 Mafumu 22:13-17 Tsono mthenga uja udakaitana Mikaya unanena naye, nati, Taona, mau a aneneri abvomerezana zokoma kwa mfumu ndi m'kamwa m'modzi; mau ako tsono afanane ndi mau a wina wa iwowo, nunene zabwino. Koma Mikaya anati, Pali Yehova, zimene Yehova adzanena nane ndidzanena ine. Ndipo atafika kwa mfumu, mfumu inati kwa iye, Mikaya, kodi tizimuka ku Ramoti Gileadi kukathira nkhondo, kapena tileke? Nati iye, Kwerani, ndipo mudzacita mwai, popeza Yehova adzaupereka m'dzanja la mfumu. Ndipo mfumu inati, Ndikulumbiritse kangati kuti undiuze zoona zokha zokha m'dzina la Yehova? Nati iye, Ndinaona Aisrayeli onse obalalika pamapiri ngati nkhosa zopanda mbusa; ndipo Yehova anati, Izi ziribe mwini, yense abwerere ndi mtendere ku nyumba yace.

Kodi inu mumakwanitsa kuyankhula zoona osaopa ?.
Kodi mumamfunsa kwandani uphungu wanu kwandani?

Mulungu akudalitseni

12/06/2021

Buku Lopatulika 1992 1 Mafumu 22:13-17 Tsono mthenga uja udakaitana Mikaya unanena naye, nati, Taona, mau a aneneri abvomerezana zokoma kwa mfumu ndi m'kamwa m'modzi; mau ako tsono afanane ndi mau a wina wa iwowo, nunene zabwino. Koma Mikaya anati, Pali Yehova, zimene Yehova adzanena nane ndidzanena ine. Ndipo atafika kwa mfumu, mfumu inati kwa iye, Mikaya, kodi tizimuka ku Ramoti Gileadi kukathira nkhondo, kapena tileke? Nati iye, Kwerani, ndipo mudzacita mwai, popeza Yehova adzaupereka m'dzanja la mfumu. Ndipo mfumu inati, Ndikulumbiritse kangati kuti undiuze zoona zokha zokha m'dzina la Yehova? Nati iye, Ndinaona Aisrayeli onse obalalika pamapiri ngati nkhosa zopanda mbusa; ndipo Yehova anati, Izi ziribe mwini, yense abwerere ndi mtendere ku nyumba yace.

Mfunso kumati inuyo pantchito yanuyo mumanena chilungamo? ,ngatitu ndi choncho kumwamwa kukusegukireni kopambana.kodi mumamfutsa kwandani uphungu wanu? Ngati mumafunsa kwa mulungu akukumbukireni .
Kodi mumayankhula zomwe ambiri anena kapena chilungamo .khalani maso inu ndi nthawi yodzuka kutulo aroma 13vs 11 .

mulungu atithandidzire ndithu kuti tidziima mu choonadi

Want your school to be the top-listed School/college?

Telephone

Website