24/02/2022
Guys pano aliyese akudziwa za kutuluka kwa ndarama yathu imodzi imene irinso yaikulu kwambiri kuposera zonse muno m,malawi ndramai ndi 5 thousand Kwacha, Ndie ndimafuna tithandizane kusova zinthu ziwiri mavuto komaso ubwino wa kutuluka kwa ndramai muno m' Malawi. Kodi ndiubwino wanji omwe ngati ife amalawi tingaupeze pakuluka kwa ndrama yaikulu chonchi nanga ndi mavuto ati omwe angadzeee kaamba ka kutuluka kwa ndrama yaikulu imenei??🤔🤔🤔 Tieni titandizane zochita tonse ndi amalawitu paja ubwino kapena zomvuta zomwe zingadze zidzakhudza tonse ngati fuko limodzi ndie sibwino kusungira zinthu kukhosi paja okhulupika adanyelera m'basitu tisaiware!!!💥💥💥