26/01/2026
THE LOST DAUGHTER πΉ
story by Meskay
πππPART ββ1
Chifukwa chani unandinamiza ,"ndinalakwa chani,zoona "analila bambo wina manja ali m'mutu ,misodzi ikutsesereka ngati mwana wakhanda.
Amayi zoona 15 years ,amayi nthawi yonseyi kundiwuza kuti ndribe bambo ,takhara tikudusa m'nthawi yowawa amayi chifukwa chani Koma "tsikana anali akuyakhula uku akasisima misodzi "
Pamalopo panali chete kwaka phindi ,palibe akafuna kuyakhura .
Amayi omwe nthawi anali asakuziwa kuti ayankhenji ,Anakhara phee kenako anagwada pasi anazayang'na mwana uja kuzapenyaso amuna awo,"Chonde mundikhulukire sindikuziwa kuti ndingayakhurenji ,ndinalakwisa ndikuvomera, pezani Malo m'tima mwanu ...
Bambo Anamukumbatira mwana wawo kwaka thawi ,onse awiri akutulutsa misodzi
Kunali zii kwaka thawi onse..........
@ story by Meskay online
Follow the our page
Next PART ...,..πΆπΆπΆπΆπ©
Real story by meskay