Malawi 24/7

Malawi 24/7 One Malawi with one goal💙

25/09/2026

Discover munthali wasimikizila komiti kuti a Ephraim Duma ndi munthu wabwino bwino alibe misala ina iliyonse

Palibe akhoza kulanditsa MCP, Ulendo okapanga deregister wayambikaChipani chokhacho mbiri yake ndiyakupha, kuononga kusa...
25/09/2026

Palibe akhoza kulanditsa MCP, Ulendo okapanga deregister wayambika

Chipani chokhacho mbiri yake ndiyakupha, kuononga kusakaza komanso kuzuza. Makolo anthu anatibisa mumadengu ife kuopa kulandila chilango kamba kosowa nkhadi.

Makolo anthu analandidwa chuma, kuthamangitsidwa mdziko muno. Ambiri ophunzila sanapeze mtendere mdziko, ochita bwino analandidwa chuma chawo. Nthawi ya MCP Mmalawi sakanakhala ndi bank, kapena hotel kulili company yopanga fertilizer dziko silikanatukuka ngati pano.

Kumbukilani anawotcha midzi iwiri ku Mangochi, imfa ya nduna zinai. Amaliwi akuti choipa chahikulu chomaliza cha MCP chikhala kupha Chilima basi. Sitingapitilire kutaya miyoyo yaanthu omwe akanapindulira dziko lathu. Mumadziwa kuti bwize bank yayamba ya Mmalawi ikanakhakhala mma 1980s? MCP inamanga bambo ake a Thom Mpinganjira kuti izi zisatheke.

Amalawi takonzeka kuchotsa mavuto pakati pathu. Ulendo uno ndi wadya mtorilo.

25/09/2026

As said when the wind changes direction the chicken a**s becomes visible, Munapheranji Chilima😩

ZOMBA CHANGALUME CONSTITUENCYMinister of Defence, Honourable Dr Feston Kaupa, M.P., who is also Member of Parliament for...
24/09/2026

ZOMBA CHANGALUME CONSTITUENCY

Minister of Defence, Honourable Dr Feston Kaupa, M.P., who is also Member of Parliament for Zomba Changalume Constituency, today attended the Zomba District Council 2026/2027 Reformed Constituency Development Fund (RCDF) Projects Launch at Chitope, Likhomomlewa, in Traditional Authority Mbiza.

The launch brought together local leaders and community members to highlight development projects being implemented under the RCDF programme for the 2026/2027 financial year.

The projects are aimed at responding to community development needs and supporting improved service delivery across the constituency.

Government launches 2026/27 FISP Minister of Agriculture, Irrigation and Water Development Roza Fatch Mbilizi has launch...
24/09/2026

Government launches 2026/27 FISP

Minister of Agriculture, Irrigation and Water Development Roza Fatch Mbilizi has launched the 2026/27 Farm Inputs Subsidy Programme (FISP), targeting 1,221,862 resource-constrained smallholder maize farmers across the country.

Mbilizi launched the programme on Thursday at Kalira 1 Primary School Ground in Traditional Authority Vuso Jere, Ntchisi District, where she said timely access to agricultural inputs was critical for farmers to make effective use of the rainfall and improve production during the 2026/27 farming season.

She said the programme goes beyond the distribution of subsidised inputs, as Government has introduced reforms aimed at improving efficiency, transparency, accountability, farmer ownership and sustainability in the implementation of FISP.

One of the key reforms is the strengthened role of Farmer Organisations, which will serve as the primary channel for beneficiary identification and input distribution.

Mbilizi said the approach would strengthen collective action among farmers, improve efficiency and enhance accountability at community level.

“We want farmers to move beyond being passive recipients of Government support. We want farmers to become organised, informed and increasingly capable of participating in agricultural programmes and markets collectively,” she said.

The Minister also highlighted the introduction of Mbeya organic fertiliser production alongside sustainable land management practices as another major reform under the 2026/27 FISP.

She said the reform seeks to address rising costs of inorganic fertiliser and challenges associated with low organic matter in soils, which affect nutrient use efficiency.

Mbilizi said the reform was also important in strengthening the resilience of the country's agriculture sector against potential climate shocks, including the threat of a mega El Niño.

Under the programme, beneficiary farmers will work in pairs to produce Mbeya organic fertiliser, with each pair expected to produce five bags of basal and five bags of top-dressing fertiliser, with technical support from extension workers.

The programme will also promote One-One planting, commonly known as Sasakawa, and other good agricultural practices aimed at improving plant population, productivity and efficient use of agricultural inputs.

Mbilizi said the choice of Ntchisi for the national launch was deliberate because the area is among places where rainfall tends to start relatively early, making timely access to inputs particularly important.

She called on farmers, traditional leaders, Farmer Organisations, extension workers, district councils, development partners, the private sector and Government institutions to work together to ensure that the programme achieves its intended objectives.

“Let us ensure that every input reaches the intended farmer. Let us ensure that every farmer uses the inputs productively. And let us ensure that the Programme contributes meaningfully to the transformation of Malawi’s agriculture,” she said.

Mbilizi commended the Ministry's technical teams, district councils, extension workers, Farmer Organisations, development partners and other stakeholders for their contribution towards preparations for the 2026/27 farming season.

She urged farmers to work towards increasing production, protecting soils, strengthening Farmer Organisations and improving the livelihoods of farming households.



LaunchesFISP

* *M’phunzitsi wa ku primary a Bertha Mlundira wayamba kuyenda m’midzi yozungulira sukulu ya Mulinga  yomwe amaphunzitsa...
24/09/2026

* *

M’phunzitsi wa ku primary a Bertha Mlundira wayamba kuyenda m’midzi yozungulira sukulu ya Mulinga yomwe amaphunzitsa kumemeza ana omwe anasiyira sukulu panjira kuti abwerere.

A Mlundira ati ataona nkhani pa tsamba la Zodiak pomwe nduna ya za maphunziro a Bright Msaka anapempha aphunzitsi kuti adzimemeza ana omwe sakupita ku sukulu kuti akalowe m'kalasi, waganiza zochitapo kanthu.

A Mlundira ati ana asungwana omwe anasiya kupita ku sukulu ku Zomba tsopano abwerera ku sukulu.

📝NEWS UPDATE

BREAKING NEWS Electricity generation and supply report of 24 September 2026 from ESCOM indicates that Malawi is not supp...
24/09/2026

BREAKING NEWS

Electricity generation and supply report of 24 September 2026 from ESCOM indicates that Malawi is not supposed to be experiencing persistent load shedding as the electrify being generated is now able to meet the demand. This now raises a question about who actually is responsible for these unexpected blackouts?? Is there any sabotage going on??

Ogwira ntchito ku Malawi Electoral Commission akhumudwa ndi mchitidwe wa Ma Commissioners a MEC pamene zawonekeratu poye...
24/09/2026

Ogwira ntchito ku Malawi Electoral Commission akhumudwa ndi mchitidwe wa Ma Commissioners a MEC pamene zawonekeratu poyera kuti ma Commissioners wa asiya kugwira ntchito yawo motsata malamulo ndipo ayamba kupanga ndale zomwe zili zosemphana ndi malamulo a ntchito! Kunyozera kwa ma Commissioners kupanga ziganizo mogwirizana ndi nthambi zaboma zapangitsa kuti ku MEC kukhale chipwerikiti ndipo ogwira ntchitowa awopseza kuti ngati ma Commissioners apitilire kupanga zawo zoduka mutu awawonetsa chomwe chinameta nkhanga mpala! Mmodzi mwa ogwira ntchito ku MEC watitsina khutu kuti ena mwa wogwira ntchito ku bungweli ayamba kale kulongedza katundu wawo kuti adzipita Ku Blantyre ndipo ma Commissioners ngati sakufuna kuwatsatira zawo zimenezo! Pali mphekesera kuti ma Commissioners ena akumalandira ntonyo kuchokera kwa eni ma warehouse zomwe zikupangitsa kuti iwo anyinyirike kusamuka

MALAWI CALLS FOR ACTION ON THE RIGHT TO DEVELOPMENTSpeaking at the UN General Assembly’s High-Level Meeting on the Right...
24/09/2026

MALAWI CALLS FOR ACTION ON THE RIGHT TO DEVELOPMENT

Speaking at the UN General Assembly’s High-Level Meeting on the Right to Development, Malawi’s Foreign Affairs Minister Dr. George T. Chaponda called for the world to move beyond declarations and take concrete action to advance development for all.

Chaponda urged reforms to the global financial architecture, greater access to affordable development finance and technology, and stronger international solidarity to address the debt, climate and economic challenges facing developing countries.

He also highlighted Africa’s critical minerals and innovation potential, calling for equitable partnerships that can drive shared prosperity.

“development must be people-centred, inclusive and equitable, and every nation must have the policy space and resources to pursue its own development priorities”, he said.

23/09/2026

Lero Hon Grace Kwelepeta MP anachititsa nsokhano ku Mikasa othokoza anthu a midzi ya Mfumu yaikulu Machinjiri mu Zomba Malosa Constituency povotera His Excellence Professor Arthur Peter Mutharika (DPP) ngati President, Iwo ngati phungu (DPP) , komanso Mai Ulemu Alfred (DPP) ngati Khansala waderali.

Mwazina, Hon Grace Kwelepeta MP auza anthu omwe anasokhana mfundo zomwe boma la MkulukutaMoyo laika pofuna kuthandiza mzika za dziko lino.

"...Ndikufuna ndikutsimikizileni kuti vote yanu ya pa 16 September 2025 simunabetse..." anatero Hon Kwelepeta.



Address

Zomba
Mulunguzi

Telephone

+265881086841

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Malawi 24/7 posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The School

Send a message to Malawi 24/7:

Shortcuts

Share