InfoNow

InfoNow Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from InfoNow, Lilongwe.

09/08/2026

During our Chanco days in times like these timati kayende

Makolokoto The Scorchers ๐Ÿซต

21/07/2026

Matching fixing kapena mchabwa ?

Tangokweza pang'ono, sindimasuka kwambiri...๐Ÿ•บ๐Ÿป
15/07/2026

Tangokweza pang'ono, sindimasuka kwambiri...๐Ÿ•บ๐Ÿป

1. Import and Export2. British American To***co (BAT)3. Sara Lee4. Press Bekeries5. Press Furniture 6. Press Transport7....
15/07/2026

1. Import and Export
2. British American To***co (BAT)
3. Sara Lee
4. Press Bekeries
5. Press Furniture
6. Press Transport
7. Press Shire Clothing
8. Kandodo
9. Admarc Fruit Canning Factory
10. Malawi Railways
11. Malawi Dairy Industry (MDI)
12. Lever Brothers
13. Bereck Power Batteries
14. Brown & Clapperton
15. Gep Shoe Company
16. Sun Batteries
17. Nandos
18. PEW
19.
20.
21.

Kunena mosabisa economy ya Malawi inayamba pakale kukhaulitsa ma company of which most of them went under in the 90's and the trend hasn't changed. Tonse tikuona zotsatira zake. Tsiku la lero munthu kapena company kufuna kudzatsegula ntchito za malonda and moreover kukhalanso M'Malawi nkuvala zilimbe komanso kulikonda dziko, the business environment is just too toxic and not conducive at all.

Mr Speaker Sir...Noted! ๐Ÿ˜€. Back then before mainstream politics, ndale za ku mpira akuziziwanso bwino mkuluyu ndipo anak...
13/07/2026

Mr Speaker Sir...Noted! ๐Ÿ˜€. Back then before mainstream politics, ndale za ku mpira akuziziwanso bwino mkuluyu ndipo anakumana nazonso๐Ÿ˜ƒ. Former Blantyre and District Football League (SRFL nowadays) Chairman and later Football Association of Malawi President, Sameer Suleiman.

10/07/2026

Current status in ๐Ÿ‡ฒ๐Ÿ‡ผ

Mighty Wanderers FC yapeza jersey sponsorship partner watsopano ya ndalama yokwana 200 million kwa chaka kuchokera ku  K...
24/04/2026

Mighty Wanderers FC yapeza jersey sponsorship partner watsopano ya ndalama yokwana 200 million kwa chaka kuchokera ku Kingbossi yomwe ndi yogulitsa njinga zamoto. Komano zikuoneka kuti ma "replica" jersey ambiri a consignment ya season ino omwe akugulitsidwa ali dominated ndi 888 bets yomwe zikumveka kuti ubale ndi noma unatha. Practically zikuthauza kuti team idzivala Kingbossi ma sapota 888 bets . Zaka ziwili zapitazo ma sapota amavala ma jersey osiyana ndi omwe ma player amavala yet pogulitsa ankati ndi ma "replica".

Ma "replica" a 888 anabwera ndi inprint yochoka ku factory and anali a season yomwe ino kusonyeza kuti sizinali zodzidzimukila. Kodi kwenikweni panavuta ndi pati kapena zimavuta pati?, Ndiye kuti 888 bets will get free advertising?, Komanso ndiye kuti aliyense obwera amafuna chizindikiro chake chidzikhala kutsogolo kwa jersey komanso large signage? Mosaphweketsa 200 mita, mwina ma team adzilola kit sponsorship ina idzipita ku training kit kapena pa arm.

Paja main sponsor wa league logo yake ikufunikanso pa front pompo ๐Ÿ˜Š

In search of long lasting peace. They have been here before ๐Ÿ‡ฒ๐Ÿ‡ผ. Mama Africa---Sad!
21/04/2026

In search of long lasting peace. They have been here before ๐Ÿ‡ฒ๐Ÿ‡ผ. Mama Africa---Sad!

The Golden Era: When MDC United Owned the Pitch. Iyi ndiye imanyapula ma team. Squad ya achina Weston Chifutwe, Clement ...
21/04/2026

The Golden Era: When MDC United Owned the Pitch. Iyi ndiye imanyapula ma team. Squad ya achina Weston Chifutwe, Clement Kafwafwa, Chiyembekezo Zidana, Grant Lungu, Heston Munthali, Mapopa Msukwa, Thango Chauma, Chrispin Mpesi and others. Inali free scoring team. On this day in 2001 mu Chibuku Cup final MDC inamenya bullets 5-2 mu regulation time.

Tsiku ili Goalkeeper wa MDC Weston Chifutwe anapambadzidwa kunkhope ndi masapota a bullets akuchoka ku dressing room pa half time khani yokhudza "juju" kapena kuti research. Mbali inayi Swadick Sanudi aniyithawa game atachinyidwa zigoli ziwili za msanga mu mphindi zosaposa 12 kuchokera kwa Grant Lungu ndipo analowa Navigator Dzinkambani yemwe naye alandiranso zake zitatu. Pofika mphindi 6 ya mu second half MDC inali itachinya chigoli cha chisanu, eee kunavumba ma botolo sizinaoneke๐Ÿ˜ƒ

Rodrick who? Gonani kaye mwatopa ๐Ÿ˜€
21/04/2026

Rodrick who? Gonani kaye mwatopa ๐Ÿ˜€

Address

Lilongwe

Telephone

+265991244425

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when InfoNow posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The School

Send a message to InfoNow:

Shortcuts

Share