22/08/2024
MWAYI MWAYI KU MLIMI ANYAMUKE INITIATIVE PAMODZI NDI KHEMA AQUACULTURE CONSULTANCY π£οΈπ£οΈ.
INTEJOIN LESSONS ON MIXED FARMING WITH MLIMI ANYAMUK INITIATIVE (MAIπ²πΌπ₯) AND KHEMA AQUACULTURE CONSULTANCY πποΈβοΈ.
Tikulengeza kuti tikhala ndi maphuziro akaphatikiza amene tidzaphuzitsa anthu ulimi wa Mbeu, Ziweto komaso Nsomba, Kukuphuzitsani momwe tingapangile ulimi osakaniza wa Nsomba, Ziweto ndi Mbeu. Pamapeto a maphunziro pazakhala gulu la azimayi ndi atsikana lomwe lizayambe ulimi limodzi ndi ANYAMUKE INITIATIVE (MAIπ²πΌπ₯) π±π komanso AQUACULTURE CONSULTANCY ππ¬
Inbox one of the below contacts ;Ngati mukufuna kupangidwa add pa group Komaso mupatsidwe ndondomeko yoyenera kutsatira.
For more: 0996058928
0881420050