Khwasu Foods and online cooking lessons

Khwasu Foods and online cooking lessons Women and youth empowerment

Kodi ndinu student, housewife, kapena tinasiya school, kapena tili ndi achibale omwe angokhara pakhomo kusowana zochita?...
05/01/2026

Kodi ndinu student, housewife, kapena tinasiya school, kapena tili ndi achibale omwe angokhara pakhomo kusowana zochita? PHUNZIRANI maluso ma ntchito yamanja monga kupanga
Sausage( 4 types)
Yoghurt osati wa flour
Cake
Bans
Swann freezes
Rainbow freezes
Doughnut
Madasi
Chapatti
Komanso mmene tigaphikire
Beef stew
Mpunga wa akini
Ndi dzina zambiri.
Zonsezi mtengo ndi Mk 20,000 yomwe mumakalipira ku training komweko
Mumangilipira registration fee ya MK 1000
Timayenda madera osiyanasiyana kuphunzitsa Anthu ndipo pa kutha pa training timapeleka machine a sausage, zakudya zomwe tapanga komanso certificate of attendance.
MA TRAINING ayamba February . Drop your numbers and location to be added ku WhatsApp groups

Order yours now
25/08/2025

Order yours now

Mwayi ophunzira kaphikidwe kamakono.Tikhara ndi online cooking lessons yomwe itazayambe pa 25 August mpaka pa 14 Septemb...
20/08/2025

Mwayi ophunzira kaphikidwe kamakono.
Tikhara ndi online cooking lessons yomwe itazayambe pa 25 August mpaka pa 14 September
Mtengo K7000
*Training outline*
Cooking 1
Cooking 2
Baking
Business tips
For K7000 only

Training ndiya online ndipo timaphunzitsa kuzera mu notes zofotokozedwa bwino mu chichewa, voice notes ndi ma guiding videos.
Register now
0884547068/0998383547.
Pamapeto pa training tizapeleka ma certificate
Anthu 50 oyambilira Kulipira azalandira free cookbooks.

https://chat.whatsapp.com/D8B8TQNrfIy8D7DcFWDpmy

23/07/2025

Shout out to my newest followers! Excited to have you onboard! John Mzee Ibotie Mwale, Bridget Wa Evaristo

Mwayi ophunzira kaphikidwe kamakono.Tikhara ndi online cooking lessons yomwe itazayambe pa 28 July mpaka pa 05 August.Mt...
22/07/2025

Mwayi ophunzira kaphikidwe kamakono.
Tikhara ndi online cooking lessons yomwe itazayambe pa 28 July mpaka pa 05 August.
Mtengo ndi K5000
Muzaphunzira
3 types of sausages
KFC chicken
Bbq wings
Peanut butter
Mango achar
Minced soya chunks
Rainbow freezes
Shepherds pie
Macaroni salad
Egg salad
Potato pizza
Goat soup
Yogurt
Maheu
Wine making
Jollof rice
Potato salad
Chocolate
Ice cream
Mayonnaise
Chigwada
And many more.
For K5000 only

Training ndiya online ndipo timaphunzitsa kuzera mu notes zofotokozedwa bwino mu chichewa, voice notes ndi ma guiding videos.
Register now
0884547068/0998383547.

https://chat.whatsapp.com/D8B8TQNrfIy8D7DcFWDpmy

Address

Lilongwe

Telephone

+265884547068

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Khwasu Foods and online cooking lessons posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share

Category