Koma kumeneko
😂😂
Education Zone
Deliver academic information to those who deserve
31/07/2026
The JCE and PSLCE examinations have been marked, and the results will be released soon. Follow Maneb Results so you can easily access the results link as soon as it is available.
24/07/2026
An IPTE 19 teacher, Alfred Chilambila, has been named Teacher of the Year at Dreamberry Private Academy in Bangwe, Blantyre.
CZ TTC SHINE WITH EXCELLENCE 🔥🔥🔥
20/07/2026
Popcorn business ndi imodzi mwa mabizinesi osavuta kuyamba chifukwa imafuna ndalama zochepa ndipo anthu ambiri amakonda popcorn.
Zomwe mungafunike
Chimanga cha popcorn
Mafuta ophikira
Shuga kapena mchere (kutengera mtundu wa popcorn)
Popcorn machine kapena poto wokhala ndi chivindikiro
Ma packet kapena ma plastic bag
Sticker yokhala ndi dzina la business (ngati mukufuna kupanga brand)
Malo ogulitsa
M'masukulu
M'misika
M'ma bus station
Pa ma event (maukwati, masewera, misonkhano)
M'mashopu kapena ma supermarket ang'onoang'ono
Momwe mungapangire phindu
Mwachitsanzo:
Mtengo wopanga packet imodzi: MK500
Mtengo wogulitsa: MK1,000
Phindu pa packet: MK500
Mukagulitsa ma packet 50 patsiku, phindu lingakhale pafupifupi:
MK25,000 patsiku
Malangizo opambana
Pangani popcorn yokoma komanso yofanana nthawi zonse.
Gwiritsani ntchito ma packet aukhondo komanso okongola.
Khalani ndi mitundu yosiyanasiyana, monga sweet, salty, kapena butter flavor.
20/07/2026
NKHANI izitha
Away from education....
Inu mwakwera it?
😂
(From inbox)
I'm in Zomba ndili ndi ma book awa english gramma bk geo complete book 3 target geo book 4 history achievers maths arise book 4 excel maths book 3 bio 3 and 4 excel agri excel 4 agri book 3 arise and ma pathlet 6 0999579539 mtengo pang'ono
19/07/2026
NKHANI YA BWINO KWA ANTHU ONSE OKHALA KU ZOMBA NDI MADERA ENA OZUNGULIRA...
Kuli holiday Classes yomwe ikuyamba pa 27 July mpaka pa 4 September 2026...Kupangira kuti mitu isazizire.
More information 👇
19/07/2026
Ngati mukufuna quality service ayeseni a ndipo Simuzakhumudwa....
FAST, ACCURATE AND RELIABLE 🔥🔥
More information 👇
19/07/2026
Nanga angalime?? Number yawo ili pompo katundu madzi uyu ..
Click here to claim your Sponsored Listing.
Location
Category
Contact the school
Telephone
Website
Address
Lilongwe