Tisathule malemba a baibulo & Qur'an

Tisathule malemba a baibulo & Qur'an

Share

Kuyankha mafuso kudzera palemba la baibulo & QUR'AN

24/02/2022

Koyambira chikrstu

Chanyambra Ku Antiokeya Anayambitsa Paulo (saulo) Machtdwe 11v25-26 Yesu Atachoka..machtdwe 1v1-2 Mateyu 24V4-5 ,23-24

17/11/2021

*Tchimo Loganizilana*

``` Amai ena amaganizila amuna awo k*ti amanyengana ndimtsikana wantchito mnyumba momwemo. Nde tsiku lina anaganiza zomutuma mtsikanayo kumudzi koma abambo saanadziwitse. Nthawi yogona itakwana, amai anapita kuchipinda mwamasiku onse ndikuwasiya abambo akuonera TV.
Atalowa kuchipinda kuja anaganiza zokalowa kuchipinda kwamtsikana ndikukalowa mubulangete ndikufunda ndikumutu komwe. Kenaka anangomva chitseko k*tsegula pang'ono pang'ono, loweni m'bulangete, popanda romance round 1, kenaka 2, kenaka 3, kenaka 4, atapsya mtima mzimayi anakweza mawu akukalipa, ''ndichifukwa chake umangondipatsa karound kamodzi kokha, umakhala utatopa ndimtsikana wantchitoyu!'' Uku akuyatsa getsi, mmaso mbeeee ataona k*ti simamuna wawo koma ndimnyamata wantchito. (garden boy) Abambo atamva phokoso kuchipinda chamtsikana, anathamangila komweko poganiza k*ti mwina kwalowa wakuba:....................... ............. Muli inu!!!!!!! Taweruzani timve```

27/04/2021

Akhristu amat or osamapanga za m'baibulo zogwetsa nkhope pans zovula nsapato mdulidwe amat bola chikhulupiliro mumtima k*tengera aroma 4v1to17? koma nd zabodza chkhulupiliro chopanda ntchto nd chopanda pake yakobo 2v14to 17,2o,,24,26 mateyu7v 24to 26 yohane 13v17 quran 85v11 komanso amat ak*t malamulo amulungu kusawachta pali kanthu bola ukudziwa k*t mulungu alipo koma nd zabodza 1yohane 2v4 tito1v 16 quran 2v8to 9

26/04/2021

Mdulidwe genesis 17v9to14 genesis 17v23to 27 genesis 21v4 machtidwe 7v8 genesis 34v12 to 17 levitiko 12v1to 3 yoswa5v2to 9pamenepo alemba k*t giligala kumasulira k*t ndagala yesaya 52v1 ezekiel 44v6to 9 luka 2v21 luka1v57to 59 yohane 7v22to 23 machtidwe 15v1 akhristu amakana mdulidwe amatenga maves awa 1akorinto7v17to 19? Aroma2v25to29?pomwe ankaletsa mdulidwe yu nd paulo agalatiya 5v1to2? Komanso paulo yo ngakhale amaletsa mdulidwe koma anadulidwa afilipi 3v3to5 machtidwe 16v1to3 aroma 15v7to 8

25/04/2021

*MUZIYAMBA MWAWONA KAYE MUNTHU YEMWE MUKUFUNA KUTI AKUCHITILENI PRINT WEDDING CARD YANU NGATI ANAPITA KU SCHOOL*
=======================
munthu wina anauzidwa k*ti pa wedding card yanga uikepo *1 YOHANE 4 vers 18*

Iye anachita mistake pochita print wedding card ija ndipo anaiwala *1* m'malo mwake anachita print *YOHANE 4 vers 18*
~~~~~~~~~~~~~~~~~~~~
*1 YOHANE 4 v 18*
```mumchikondi mulibe mantha popaza chikondi cheni cheni chimachotsa matha onse```

*POMWE YOHANE 4 v 18 AKUTI*
```pak*ti wakhala nawo amuna 500 ndipo mamuna yemwe ulinaye pano siwakonso```
😂😂😂😂😂😂😂
___________________________
*Masana abwino guys*

24/04/2021

Maves omwe amaletse wivi ndi awaa yelemia 4:30
2 mafumu 9vs30-34
1petulo 3:3-4

Mkazi asalalikire kapena kulankhula mu church
1 akolito 14:34-35

Kusamalira nkhalamba mphuzits 9;4
Miyambo 26:14

Kuvala mpango popephera
1 akolito 11:5-6
" 11:13
Genesis 24:64-65

Mkaz asavale
chamuna deternomo 22vs5

Zonkhutsa kumeta mmbali tsitsi
Yeremia 9:25-26

Want your school to be the top-listed School/college in Lilongwe?

Click here to claim your Sponsored Listing.

Location

Category

Website

Address


Salima
Lilongwe