Luso Technical college

Luso Technical college Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Luso Technical college, Area 3 near NBS and Area 1 White falls, Lilongwe.

MAPHUNZIRO OSAFUNA CERTIFICATE KUTI MUTENGEDWE AKUYAMBA PA 7 SEPTEMBER 2026 KU LILONGWE & BLANTYRE.LUSO TECHNICAL COLLEG...
12/08/2026

MAPHUNZIRO OSAFUNA CERTIFICATE KUTI MUTENGEDWE AKUYAMBA PA 7 SEPTEMBER 2026 KU LILONGWE & BLANTYRE.
LUSO TECHNICAL COLLEGE

yomwe ndi school yantchito za manja, yakonza maphunzirowa ngati njira imodzi yolimbikitsa anthu kuyamba ma business awo osati kudalira kulembedwa ntchito kokha ndipo maphunzirowa ali m'magawo awiri pofuna kupereka mwayi kwa aliyense kuti aphunzire posatengera maphunziro anu.

GAWO LOYAMBA - LOMWE LIMAKHALA 100% PRACTICALS (INFORMAL)
- Lomwe aliyense atha Kuphunzira bola mukhale mumanva komanso kulemba English.

GAWO LACHIWIRI
- Formal courses - lomwe timalola omwe ali ndi certificate ya form 2 kapena form 4.

KUTI MUTENGEDWE MUKAPHUNZIRE PANGANI IZI:

- onetsetsani kuti mwasankha mwanzeru pama course omwe taikawa (posters) poti ili ndi tsogolo lanu.

- imbani phone or WhatsApp pa: 0995545449/0888114412 kuti mulandire form yolembetsera olo muli kwanu.

Maphunzirowa amakhala awunikidwa kale potengera ubwino kwa ophunzira akamaliza school kuti atha kumapanga ndalama mosavuta.

MUTHANSO KUSINDIKIZA LINK ILI MMUSIYI KUTI MULEMBETSE
The link is https://lusotechnicalcollege.com
OR
MUTHANSO KUFIKA KUMA OFFICES OMWE ALI:
LILONGWE: Area 3 behind NBS bank.

BLANTYRE: Limbe mu City Plaza building flow number 3, yanakis.
Nb: Malo ogona alipo kwa onse akutali omwe m'malipira padera ndipo akuyambira k45,000 -K70,000 Pamwezi ndipo chakudya ndi chanu. onetsetsani kuti malo mwalipirilatu musadapite ku school.

KUTI MUTSATIRE ZONSE PANGANI LIKE FACEBOOK:

10/08/2026

Mavuto azachuma tilinawowa adzachepa ndithu!!! Ngat mutasankha Kuphunzira ma awa.

Ndalama pang'ono koma zingwinjiri mbwee!!.

The link is https://lusotechnicalcollege.com

Learn, Grow and Lead with Us!
05/08/2026

Learn, Grow and Lead with Us!

02/08/2026

kuti muphunzire course ya PLUMBING ndizosavuta sindikizani link ili m'musiyi ndipo sankhani APPLY NOW kenako yankhani mafunso molondola.

The link is https://lusotechnicalcollege.com

30/07/2026

Pa 3 AUGUST TIYENI!.

Kwacha tiziyambitsepo ntchito za manjapowered by
27/07/2026

Kwacha tiziyambitsepo ntchito za manja
powered by

Next week! Episode 1.
18/07/2026

Next week! Episode 1.

18/07/2026
18/07/2026

Sizibisaso pano kuti anthu azindikila kapena anthu amene amamvetsa bwino school ya za Hotela kapena yozasamalira alendo akumabwera kuzaphuzira ku Luso Technical College.

Lembetsani lero nanu ndipo mykhale nawo mu guru ya anthu ochitabwino ndimaphunziro.

Technical College
agent of change

Address

Area 3 Near NBS And Area 1 White Falls
Lilongwe
259

Telephone

+265995545449

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Luso Technical college posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The School

Send a message to Luso Technical college:

Shortcuts

Share