Malawi Daily

Malawi Daily This Creative Centre is here to educate and inform guardians on different aspects concerning childre

INE NDI NDANI....? ❤️
28/12/2024

INE NDI NDANI....? ❤️

🚨Heartbreak of the year...💔Basitu woyimba wamkazi, Hezel Mak, angomusiyira mwana kenako mamuna wawuyatsa ulendo, banja l...
28/12/2024

🚨Heartbreak of the year...💔

Basitu woyimba wamkazi, Hezel Mak, angomusiyira mwana kenako mamuna wawuyatsa ulendo, banja latha.

Pepa, Hezel. Heaven is the goal!

Apa walowa gulu lama single mums lachina Miracle Chinga, Tamia Ja…

Mpangeni tag mwini nkhaniyi
28/12/2024

Mpangeni tag mwini nkhaniyi

23/12/2024

Madeya ayambile panja mpaka nyumba mwanumo Nkhuku ikalowa sekani chitseko,,,mapezedwe a Mpunga tiphunzitsana mawa... Xmas🎅

Oimbila mpira wamiyendo okwana khumi asanu ndi mmodzi avomelezedwa ngati a FIFA a dziko lino.Pa oyimbilawa pali Godfrey ...
21/12/2024

Oimbila mpira wamiyendo okwana khumi asanu ndi mmodzi avomelezedwa ngati a FIFA a dziko lino.

Pa oyimbilawa pali Godfrey Nkhakananga, Easter Zimba, Mayamiko Kanjere ndi David Chinoko.

Kumbali ya othandizira ndi Bernadettar Kwimbira, Clemence Kanduku, Pondamali Tembo, Happiness Mbandambanda, Evance Msonda, Lameck Phiri, Samuel Fudzulani, Mphatso Matete ndi Sibusiso Sibande.

Koma kumbali ya oimbila omwe akhoza kumaunika nawo pa kanema (VAR) palibe yemwe watengedwa mdziko muno kamba koti Nkhakananga, Gumbo ndi Tembo onse akanika.

Rose Zimba wakanika kukhala nawo pamndandanda wa FIFA.

Zabwino zonse

Congratulations to Mighty Mukuru Wanderers FC  for being crowned the 2024 Castel  Challenge Cup Champions.
21/12/2024

Congratulations to Mighty Mukuru Wanderers FC for being crowned the 2024 Castel Challenge Cup Champions.

Bad day for the Cities⚽
21/12/2024

Bad day for the Cities

⚽

Mozambique ndi chifukwa chimene chimachititsa kuti Tanzania izifuna mbali ina ya Nyanja ya Malawi. Tikuganiza izi chifuk...
20/12/2024

Mozambique ndi chifukwa chimene chimachititsa kuti Tanzania izifuna mbali ina ya Nyanja ya Malawi. Tikuganiza izi chifukwa mbali ina ya nyanjayi ndi ya dziko la Mozambique. Chifukwa choti tinatema kumupatsa neba (Mozambique) naye neba winayu (Tanzania) amafuna titamutemere.

Kumbukirani kuti ngakhale boma la Likoma ndi limodzi mwa maboma a ku Malawi koma bomali limapezeka mbali ya nyanja yomwe ili m'manja mwa Mozambique. Ichi ndi chifukwa chake mzere osonyeza malire a dziko la Malawi ndi Mozambique (international boundary line) umaoneka kuti unadutsa m'nyanja ya Malawi.

18/12/2024

Just because he dated u for 4 good years doesn't means he will marry u.
My uncle study medicine for 8 years and he is a DJ now.

14/12/2024



Entertainers of the Year— music category winners

Male Secular Artist of the Year
Driemo

Female Secular Artist of the Year
Emmie Deebo

Male Gospel Artist of the Year
Steve Wazisomo Muliya

Female Gospel Artist of the Year
Miracle Chinga

Secular Song of the Year
Kutali by Fadda Motti

Mutawapeza mungawatani
13/12/2024

Mutawapeza mungawatani

Jetu akupuma kuyimba chaka chamawaOyimba wachikulire, Jetu adzasiya zoyimbayimbazi chaka chamawa. Dyokhwe, m'modzi mwa a...
13/12/2024

Jetu akupuma kuyimba chaka chamawa

Oyimba wachikulire, Jetu adzasiya zoyimbayimbazi chaka chamawa. Dyokhwe, m'modzi mwa adzukulu ake a Jetu, watsimikizira za nkhaniyi.

Iye wanenetsa kuti kaya aMalawi mufune kaya musafune koma Jetu akupumila zoyimbazi chaka cha 2025. Mkufotokoza kwake, wati Agogo akewa akudzapuma kuyimba chifukwa akalamba kwambiri.

Pakadali pano, Jetu yemwe ali ndi zaka 73, watulutsapo nyimbo zingapo zimene zikusangalatsa anthu monga, Wakalamba Wafuna, Chakwaza, Simunatchene imene anayimba ndi m'dzukulu wakeyu ndi zina zambiri. Jetu watulutsaso nyimbo ina yotchedwa 'Waimanya' masiku anayi apitawa imene anthu akuikondaso kwambiri.

Address

Lilongwe

Telephone

+265991340187

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Malawi Daily posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The School

Send a message to Malawi Daily:

Shortcuts

Share