Yesu ndi yankho

Yesu ndi yankho Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Yesu ndi yankho, Tutor/Teacher, Box 20 mpepa Kasungu, Kasungu.

27/05/2023

Mulungu amakonda aliyense amene amamuvera ndi kuchita chifuniro chake

27/05/2023

Mukhale ndi chidziwitso pakupanga zinthu

27/05/2023

ana anu makhalidwe abwino awapatse mulungu mu dzina la Yesu Khristu mwana wa Mulungu wa moyo

27/05/2023

Mulungu mutigonetse tulo ta bwino

02/05/2023

Ndiyamika yehova wanga olenga kumwamwa ndi dziko olenga iweso ndi ine

17/03/2023

Tiyeni tiwerengere limofzi pa aroma 8vs12 pomwe akuti 12Cifukwa cace, abale, ife tiri amangawa si ace a thupi ai, kukhala ndi moyo monga mwa thupi; 13pakuti ngati mukhala ndi moyo monga mwa thupi, mudzafa; koma ngati ndi mzimu mufetsa zocita zace za thupi, mudzakhala ndi moyo. 14Pakuti onse amene atsogozedwa ndi Mzimu wa Mulungu, amenewo ali ana a Mulungu, 15Pakuti inu simunalandira mzimu wa ukapolo kucitanso mantha; koma munalandira mzimu waumwana, umene tipfuula nao, kuti, Abba, Atate, 16Mzimu yekha acita umboni pamodzi ndi mzimu wathu, kuti tiri ana a Mulungu;

17/03/2023

Mulungu wakhala thandizo ponitandiza machitidwe onse kuti nditsekure peji ili tikhala tikuphuzira mau a mulungu pano mulungu azikudalitsani ngati mwapanga like or following my page

Address

Box 20 Mpepa Kasungu
Kasungu

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Yesu ndi yankho posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share

Category