Opani kuimba komaso kugawa nyimbo
Awa nd machimo amene amakulitsabe chilango chako ngakhale utamwalira chifukwa umazisiya pa dziko lapansi zikuonongabe dziko. Unawaila aja akumverabe kapena akugawa kwina.
Finally siyani kumvera Nyimbo!!
ICBM DAWAH CLUB
Lets Learn, Teach and guide the ummah in the way of Islam
مَنْ صَلَّى فِي يَوْمٍ ثِنْتَىْ عَشْرَةَ رَكْعَةً تَطَوُّعًا بُنِيَ لَهُ بِهِنَّ بَيْتٌ فِي الْجَنَّةِ "
Hadith
Narrated Umm Habibah:
The Prophet (ﷺ) as saying: If anyone prays in a day and a night twelve rak'ahs voluntarily (supererogatory prayer), a house will be built from him in Paradise on account of these (rak'ahs).
Sahih (Al-Albani)
Sunan Abi Dawud 1250
In-book : Book 5, Hadith 1
English translation : Book 5, Hadith 1245
Abu Dawood
Ukamagawa uthenga wa choonadi kwa anthu ofooka chikhulupiliro amakuyankha👇👇
"Lalikiran zoyanjanitsa osat k*tigawanitsa"
Kod munamba mwalingalirako k*t inu ndamene mumatigawanitsa potuluka mwaife?
Ndithu sali mwaife amene angabwere nd chopeka Bidia
Zakatul fitr iperekedwe before swalah ya Eid ndipo tipereke chakudya chodyedwa ku dela lomwe tikupelekalo... chakudya not ndalama ngat muli nd ndalama zambiri kagulen chakudyacho(chimanga or mpunga) nachipereka
Funso
Munthu akufuna kupanga banja(sex) mu nthawi ya Swaum ndye wamasula kae kenako kupanga, Kod nae akuenera (kuzasala 60days)
Answer
Yes azabweze tsikulo and 60days كفارة chifukwa wapanga exposure Haram ya mwez wu
أراد أن يجامع في رمضان، فأكل قبل الجماع هل عليه كفارة؟؟
يجب كفارة لأنه هتك حرمة شهر
(الجمهور)
(جامع العام الأحكام صيام، ص ٢١٧)
الحديث
من ترك الصلاة عمدا فقد كفر.
(Hadith)
"amene angasiye swalah mwadala, ndithu iye wakanira"
ndukuchenjezani za kuswalih, tisamangosala osaswali. simatheka swaumu kwa okanira, chonde mpembedzen ambuye wanu ndipo mangan maubale
الحديث اليوم
قال رسول الله صلى الله عليه وسلم : (من نسي وهو صائم فأكل أو شرب، فليتم صومه فإنما أطعمه الله وسقاه)
رواه مسلم
Mtumik wa Allah S. A. W adat:
Kwamene wasala ndkudya komanso kumwa moiwala, akuyenera apitilize swaum yake ndithu ndi Allah amene wamudyesa iye ndkumumwesa.
Mu hadith imenei ak*t kuiwala. Kuiwala kulibe mankhwala komanso kuiwala samachita kukonza
Allah alandire kusala kwathu
Assalam alykum warahmatullah wabarakatuh
Ndichan mungakonde k*t tizikubwereseran PA page pano mu nthawi yokolora ya Ramadhan
May Allah accept our fasting, ameen
Hadith
Lesson 11
Hadith
حَدَّثَنَا الْحَسَنُ بْنُ عَلِيٍّ، حَدَّثَنَا عَبْدُ الرَّزَّاقِ، أَخْبَرَنَا مَعْمَرٌ، عَنِ الزُّهْرِيِّ، عَنْ أَبِي سَلَمَةَ، عَنْ أَبِي هُرَيْرَةَ، عَنِ النَّبِيِّ صلى الله عليه وسلم قَالَ
مَنِ اتَّخَذَ كَلْبًا إِلاَّ كَلْبَ مَاشِيَةٍ أَوْ صَيْدٍ أَوْ زَرْعٍ انْتَقَصَ مِنْ أَجْرِهِ كُلَّ يَوْمٍ قِيرَاطٌ "
Narrated Abu Hurairah:
The Prophet (ﷺ) as saying: If anyone gets a dog, except a sheeping or hunting or a farm dog, a qirat of his reward will be deducted daily.
Galu Sali ngat zinyama zinaz za pakhomo choncho tisawete agalu popanda zifukwa monga uzimba Nd zifukwa Zina zofuna galu, chifukwa kungomuweta ngt chiweto chapankhomo amachotsa ma Baraka anu
Sunan Abi Dawud 2844
In-book : Book 17, Hadith 1
English translation : Book 16, Hadith 2838
Abu Dawood
Kodi mwalonjezedwa k*t mawa mulifika?
Let's Change its not too late
May Allah bless you All!!
Hadith
Lesson 10
عن أبي هريرة رضي الله عنه قال: قال رسول الله صلى الله عليه وسلم :
لا يحل لامرأة تؤمن بالله واليوم الآخر تسافر مسيرة يوم وليلة إلا مع ذي محرم عليها"
((متفق عليه))
Abu Hurairah (May Allah be pleased with him) reported:
The Messenger of Allah (ﷺ) said, "It is not permissible for a woman who believes in Allah and the Last Day to make a journey of one day and night unless she is accompanied by a Mahram (husband or any other relative to whom she is prohibited to marry)."
*sizololedwa(Haram) kwa mzimayo wokhulupilira mwa Allah Nd tsiku lomaliza kuenda ulendo okwana tsiku pokhapokha akhale Nd maharam(mamuna wake kapena wa chibale yemwe sangakwatirane naye*
[Al-Bukhari and Muslim].
Sunnah.com : Book 8, Hadith 34
Arabic/English book : Book 8, Hadith 989
Riyad us Saliheen
Milaad Nabiyy???
Kukubukira kubadwa kwa mtumik palibe dipo Lili lonse kupatula moto
كل محدثة بدعة و كل بدعة في النار
Ndipo izi zosangalala nd Zina mwa zopeka mchipembedzo
وعليكم بسنتي و سنة خلفاء الراشدين umenewo Nd Umboni okwanira kwa amene Allah wamuonesa chiongoko
Mwiniwake Ali moyo sadapange makhalifa sadapange ma tabiu sadapange ma tabiu tabieena sadapange... Who are u?? Umboni ndapereka wo Nd mau ochokera kwa mtumik k*t *tsatilan ine komanso MA Khalifa* nde onsewo sadapange inu mutsatira ndan???
Click here to claim your Sponsored Listing.
Location
Category
Telephone
Website
Address
Blantyre