Ntata Primary School Student.

Ntata Primary School Student.

Share

Ntata primary school

01/04/2026

Shout out to my newest followers! Excited to have you onboard! Tiyamike Mwana Wasalubeni, Manuel Lampa

19/12/2025

Moni abale nonse komwe muliko chifukwa Cha kupempha kwa gulu akuti tikhale ndi Whatsapp group sindikuziwa inu mukutipo bwanji ndiona ndi kuchuluka kwa anthu ofuna kuti zitero ndatha ine addm anu.

05/06/2025
05/06/2025

Azanga nonse omwe taphunzira pa ntata fp xool please tiyeni tionekele ku gulu M'bale wina anapeleka chi list Cha abale omwe anaphu tinaphunzira pa xool yathu yokodedwa ngt abale ena mwawasowa tiyakhuleni mwina ndikuthandizana kuwapeza

16/11/2023

Pamene chiwelengelo cha Anthu omwe anaphunzila pa Ntata school chikukwela daily and pano tili Mu 17k ndafuna kupempha azathu omwe ali ndi kuthekela kothandiza pa school kuthandizatu sikuti ndi zambili ai chili chonse chomwe ungathe zilimbikisa ana omwe akuphunzila pa school ndy ngt Mulipo please tiyakhuleni kt uthengawu tiufalise kt Ena atengelepo chisazo zikomo.

22/03/2023

Hello amalawi Azanga Choyamba ndipepese potenga nthaw osaonekela kwa anthu Komanso ndiyamike Mulungu ponditeteza ku cyclone Freddy namodwe ameneyu waononga kwambili Ndiy zonse akudziwa ndi Mulungu Pali anthu omwe akhala a kupempha kt tikhazikise group pa whatsap kt tizitha kukambilana nkhani zathu Komas kuziwa momwe moyo wathu ulili ndy kwa omwe anaphuzila pa ntata please hala me pa nambala iyi kt ndikuchiteni add pa group ya ntata cool 0881877464 kwa ofuna not kakamiza Zikomo.

03/11/2022

Ndikufuna Ndithokoze anthu Onse omwe atengapo mbali ena akumbukila nthaw Yao ena zawakumbusa maluso omwe anali nao pa school yathuyi school iyi anthu ochuluka yawapindulila ena ndi ma Bwana pomwe ena ma minister koma palibe Yemwe ananganizilapo zofuna kuthandizapo PA cool yathuyi chonde tiyeni tiinganizilenso school chithandizo sichichepa even makope o so kwa omwe akufuna kwabwino khomo ndilosengula tiyeni tichitepo kanthu pofuna kutukula school yathuyi Zikomo.

22/07/2022

Ndikufuna kuthokoza anthu Onse omwe mukutengapo mbali PA group yathu ya Ntata chonyandisa china ndi chakuti nditha kusimikiza kt mbuyomu Grecian phiri amafunafuna a Mbale ake Kuno kumalawi iyeyu amakhala ku Botswana ndp munthu yemwe amafunikayu ndi Susan Dausi phiri mwachisomo anthuwa akumana sopano mokuti nthaw ina iliyonse anthuwa akhala akubwela Kuno ku Malawi izi zitheka ndi Ntata xool ndikufunilani Zabwino ambuye akundaliseni zikomo.

01/05/2022

Lady's and Gentlemen I believe that both of you your are fine I also want to appreciate everyone's who take part in this group God bless the aim of this group is to know you and the year you learn at this school who was your head teacher? Your class teacher? And I have a request to you all Mrs Milazi is also the one who follow this school but as of now she is in Botswana so she request each and everyone who have a phone number of Mr sigara this one was a teacher at ntata school and every one who have got phone number please share it to this school I hope we will help her God bless you all.

02/10/2021

Pali ndongosolo la trip yopita kukaona school yathu ya ntata komaso tikupemphedwa kungula mphatso zokaonela ana omwe ali pasukulupa ndy ma coment anu ndi omwe apangise kt trip ichitike komaso ulendo uyambika from bt thank.

Want your school to be the top-listed School/college in Blantyre?

Click here to claim your Sponsored Listing.

Location

Category

Telephone

Website

Address


Bangwe
Blantyre