15/04/2026
*MALAWI ISLAMIC ARTS*
Malawi Islamic Arts ndi tsamba lomwe limathandiza Achinyamata aluso kuti afikile anthu ochuluka mukamphindi kochepa ndipo ndi tsamba lokhalo la pa internet lomwe lili ngati nkhokwe yopezela mitsangalutso yosiyana siyana komanso Zina zokhudza Chikhululupiliro Cha Chisilamu.
Monga mukudziwa tsambali limapezeka ndi zinthu Monga:
- Ma Ulaliki (Bayan)
- Quran (yotanthauzila muchichewa komaso Chizungu
- Ndakatulo
- Ma Nasheed
ndizina zambili.
Pakufuna kupitiliza ndi zintchito zimenezi komaso Kuthandiza Achinyamata aluso muno MMalawi, tsopano pa tsambali Achinyamata Aluso atha Kutsekula account yomwe iziwapatsa mwayi opanga:
1. Kuika zinthu pa Internet (Mwaokha
2. Kugulitsa komaso kukhazikitsa mitengo ya Ma luso awo
3. Kuona momwe Maluso awo akuchitila patsambali monga kuona chiwelengelo Cha ovela, Ogula komaso omwe apanga download Maluso awo.
4. Kutha kulumikizitsa zinthu zawo ndi tsamba la *YouTube* kuti zisavute kagawidwe.
Zakhale nafe Limodzi pa Mkumano wapa Internet omwe tizakhale tikuonetsa kaonekedwe Ka tsopano Ka website komanso Kuphunzitsa kapangidwe upload kazinthu zanu.
Tsikundi pa *25 April* kudzera pa *Google Meet.*
Kuti mudziwe zambili tipeze pa
WhatsApp: +265 998 737 873
Malawi Islamic Arts
Provision of dhikr through Arts
15/04/2026
Website yanyuwani pa 25 Epulo pano
Zomwe website yanyuwani idzichita
*kupanga upload nokha ma nsheed anu ndi ndakatulo komanso ma video
*kugulitsa luso lanu (nasheed,ndakatulo, ma video) pa mtengo okhumba kumtima kwanu
Tiyeni pa 25 April nthawi ya 8koloko madzulo ma artist tiphunzile mmene tingapangile upload komanso kugulitsa luso lathu
Link to join WhatsApp group
https://chat.whatsapp.com/FL42ZHymouiKcSC1qJS6bf?mode=gi_t
09/03/2026
Ulaliki wa mitala nde Mweeetu!!! Mano onse 40 panja.
Koma akati abaya 210 pin kuipitsa Nkhope ngati akumetani.
13/02/2026
1. Solomon ...... 700 wives + 300 concubines
2. Rehoboam ...... 18 wives + 60 concubines
3. Abijah ...... 14 wives + concubines
4. David ...... 8 wives + multiple concubines
5. Jacob ...... 4 wives
6. Esau …..... 3 wives
7. Abraham...... 2 wives + 1 concubine
8. Elkanah …..... 2 wives
9. Lamech ...... 2 wives
Kumawelenga Baibulo mwanzeru👀
Polygamist men were literally the foundation of the Bible and they all found favor in the eyes of God.
Abraham, Jacob, David & Solomon - The Bible’s Polygamy Stories They Don’t Tell You.
Enewe good night🤓
08/02/2026
Tili mu mwezi wa ma Nikkah a Fast Fast!!
02/02/2026
Mafayilo atsopano omwe atulutsidwa okhudza Epstein waku america akuonetsa ma email omwe akufotokoza za kutumizidwa kwa nsalu yopatulika yochokera ku Kaaba ku Makkah, nsalu zi zinaperekedwa ndi ku gulitsidwa kwa Jeffrey Epstein, yemwe ndi olemera kwambiri komanso anali ndi mulandu wo gwiririra.
Maimelo amenewa, olembedwa mu February ndi March 2017, akusonyeza mayi wa bizines dzina lake Aziza Al-Ahmadi ankagwira ntchito ndi Abdullah Al-Maari zokhudzana kumugukitsa epstein nsalu yakuda yokongoletsedwa ndi golide yomwe imaphimba Kaaba, malo opatulika kwambiri mu Chisilamu ku Saudi Arabia.
01/02/2026
Ma muslim sisters oyika ma nails inu,
Nde mwati Istinja mmapanga bwanji??
😂😂😂😂😂😂😂😂😂
30/01/2026
Every Muslim parent should teach their children this five things 👇
1. Tawheed
teach them to know Allah, love Him, and rely on Him.
"Whoever Allah guide, none can misguide him."
Quran 39:37)
2. Ṣalāh
Make prayer a habit before it becomes an obligation.
“Command your family to pray and be steadfast in it.” (Qur’an 20:132)
3. Good Character (Akhlaq)
Manners before knowledge. Kind words, honesty, mercy.
“The best of you are those with the best character.” (Hadith – Tirmidhi)
4. Halāl & Ḥarām Awareness
Teach them what pleases Allah and what displeases Him.
“O my son, even if a deed is the weight of a mustard seed…” (Qur’an 31:16)
5. Love for the Qur’an & Sunnah
Let the Qur’an be their companion, not just a book.
“The best of you are those who learn the Qur’an and teach it.” (Bukhari)
Reminder for parents:
Children learn more from what we do than what we say.
O Allah, rectify our offspring and make them the comfort of our eyes. Āmīn
Sister Saratu Yahaya
12/01/2026
Chete kuyang’anira kumanga mzikiti