The Wolves

The Wolves

Share

WE HERE FOR YOU

25/06/2024

We are happy to inform you that we now have our own septic truck. Pumping sewer will now be quick and affordable.

25/04/2024

Anawa amakhala munsewu mu nzinda wa blantyre ku limbe. Titawafufuza tinapeza kuti mavuto awo ndi chakudya, pogona, zovala ndi mwayi wopita ku school. Wang'ono alindi dzaka 3, wamkulu alindi 6.Hope for children trust yaganiza yowachosa anawa munsewu ndikuwapasa zosowa zawo kudzela mwainu anthu akufuna kwabwino.

21/01/2024

Timakodza ma toilet odzadza pa mtengo wotchipa ndipo okambilana. Mukatifuna imbani pa nambala iyi. 0881060639

27/11/2023
Photos from The Wolves's post 21/11/2023

One of our project in progress.

Photos from The Wolves's post 18/11/2023

Call us on 0881060639

18/11/2023

Timaika ma Celling mu nyumba mwanu. Pa mtengo wotsika ndipo okambilana. Tiimbileni pa # 0881060639

18/11/2023

Timaika ma Celling mu nyumba mwanu. Pa mtengo wotsika ndipo okambilana. Tiimbileni pa # 0881060639.

17/11/2023

Tili ndi azimisili aukadaulo ndipo ozisata omanga ma nyumba pa mtengo wosika kwambili ndipo okambilana. Kwama kasitomala athu a pulani ya mtengo wotsikilako musaope musakaike. Tikumanga ma nyumba a chipinda chimodzi, ngalande, ntchito ilionse ikugwilidwa

Want your school to be the top-listed School/college in Blantyre?

Click here to claim your Sponsored Listing.

Location

Telephone

Website

Address


Blantyre