Islam Dawa

Islam Dawa Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Islam Dawa, Religious school, khodomapata@gmail. com, Blantyre.

23/12/2024

Mnyamata amene akuyesera Kulimbikisa asilamu Kuti adzitsatira
Quran Yokha ponena Kuti Quran ndiyokwanira, Tikatengera ndime zomwe zili mu Quran monga izi

6:114-115 /16:89/17:89/2:2/5:3/6:38/4:82/10:37/10:32/55:1-2

Werengani verse ili ndipo Mulumikize ndizimene mnyamatayu amayankhula

Suurat Al-Maa'idah (5:54)

يَا أَيُّهَا الَّذِينَ آمَنُوا مَن يَرْتَدَّ مِنكُمْ عَن دِينِهِ فَسَوْفَ يَأْتِي اللَّهُ بِقَوْمٍ يُحِبُّهُمْ وَيُحِبُّونَهُ أَذِلَّةٍ عَلَى الْمُؤْمِنِينَ أَعِزَّةٍ عَلَى الْكَافِرِينَ يُجَاهِدُونَ فِي سَبِيلِ اللَّهِ وَلَا يَخَافُونَ لَوْمَةَ لَائِمٍ ۚ ذَ‌ٰلِكَ فَضْلُ اللَّهِ يُؤْتِيهِ مَن يَشَاءُ ۚ وَاللَّهُ وَاسِعٌ عَلِيمٌ ﴿٥٤﴾
54. 'E inu amene mwakhulupirira! Amene Mwa inu asiye chipembezo chake, Ndiye kuti posachedwapa Mulungu Adzabweretsa anthu omwe Awakonda, nawonso amkonda; Odzichepetsa kwa Asilamu anzawo; Amphamvu kwa osakhulupirira; Omenyera nkhondo chipembezo Cha Mulungu, saopa kudzudzula Kwa odzudzula. Umenewu ndi Ubwino wa Mulungu; amaupereka Kwa amene wamfuna. Ndipo Mulungu ndi Mataya; Ngodziwa kwambiri.







27/05/2024

Chisilamu ndichiyani?

12/02/2024

potengera vesi ili Quran_13:38 anali ndi nkaza komanso ana

Address

Khodomapata@gmail. Com
Blantyre

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Islam Dawa posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share