16/01/2024
2007 Nissan bluebird inbox
Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Zokonda amai komanso abambo, Chiwembe P. O BOX 32, Blantyre.
16/01/2024
2007 Nissan bluebird inbox
14/01/2024
5pin basi
Zizayenda part 1
It was morning 8 o'clock pamene ndinayitanidwa ku office ya head master anandiuza k*ti ndipakile katundu wanga ndipo ndizipita chifukwa school yawo sinali ya ulere Nnawayang'ana mwa chisoni but anandikuk*tila Mano ndithu mokhudzika nnangotuluka uku ndikulira mmh ðŸ˜
Tiyambe ndi chonchi Ndine Naomi kwathu ndi ku chikwawa ndili form 2 ndimaphunzira ku mulanje makolo anga ndiwosawuka ndithu Mayi anga amalima zinthu zosiyana siyana amapanga izi k*ti azitikwanisa k*tisamalira Ndine oyamba kwathu pa ana atatu bambo anga amangokhalira kuledzera komanso akazi koma mayi anga amakonda ndithu
Pachifukwa choti bambo agulisa zipatso zonse ndalama ndikumwera mowa ndeno amayi sakwanisa kulipira sukulu fizi yanga ulendo uno. Okay let's continue nnafika ku hostel ndipo nnayamba kulira kenako nnalongeza zovala ndi ma buku anga k*ti ndikupita basi.
Next part tomorrow I'm tired 😀
11/01/2024
Inbox
Pali mkazi winawake 21 years ATI akufuna blesser ku inbox 🤣ma blesser nazoni kanyama kabwino kabwera kokha
I'm in relationsleep💚
Phuma njeee 😂
Welenganiso bwino 🤣
Have you been in a relationship where you feel like you are just fórcing your partner to love you 🥹😒
2years osamwako fanta anthu mulungu panganipo kanthu chonde 🤦
Zikomo popanga zokonda amai ndi abambo . Osat amai okha timaona k*ti amai okha okha amango tukwanana opanda kunenapo chanzelu ai . Kungonyoza ndi kunyodola anzao apamitala nao . Apa mwaganiza bwino k*t tiziuzana molakwika olo ife amuna timauzana moyenela pomwe amai ai kunyozana .
Tay grin woyeee 🤣