Voice of prophecy Bible School in Chichewa

Voice of prophecy Bible School in Chichewa To provide Bible trueth through Bible trueth and teachings.

01/05/2025

Pa vesi 115 paja akutionesa zomwe zimatilepheresa kuti kuunika kwa panjira zathu ndi kukhala nyali zomwe mafuta alimo okwanira kufikira kudza kwa Mkwati adzifotokoza bwino ndithu

01/05/2025

Buku loposa mabuku onseli limamuunikira munthu wina aliyense mmene angayendere mokhulupirika komanso njira zake zonse zimakhala zoongoka zokha zokha

01/05/2025

105Mau anu ndiwo nyali ya ku mapazi anga,

Ndi kuunika kwa panjira panga,

01/05/2025

Tiyeni timve pa Masalmo 119:105

01/05/2025

Buku lolimeneli ndilimene lili ndi malamulo a Yehova

01/05/2025

115Mundicokere ocita zoipa inu;

Kuti ndisunge malamulo a Mulungu wanga.

01/05/2025

Werengani Masalimo 119:115

01/05/2025

Kodi buku loposa mabuku onse ndi litilo?

29/04/2025

Katundu wanu wa ucimo mumusezese Yesu Khristu kuti alunyamulireni zothodwetsa zanu. Pakuti anati " ldzani kwa lne nonse olema ndi othodwa ndipo ndidzakutulani akatundu anu, senzani goli langa popeza lili lopepuka"

29/04/2025

Yesu Khristu anati ' lne ndine njira, coonadi ndi moyo.Okhulupirira lne angakhale amwalira adzakhala nao moyo osatha.' Kodi iwe ukhulupirira zimenezi ?!

23/04/2025

Yohane 7 vesi ya 32

23/04/2025

Tiyamba kuphunzira maphunziro athu akupeza kuyambira pa 1 May, 2025 . Cotero dziwani kuti muli olandiridwa ku sukulu imeneyi

Address

Mugabe
Blantyre

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Voice of prophecy Bible School in Chichewa posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The School

Send a message to Voice of prophecy Bible School in Chichewa:

Shortcuts

Share

Category