25/06/2026
KUBWERERA KUNYUMBA SI KULEPHERA, NDI MWAYI WOYAMBIRANSO.π²πΌπ²πΌ
Mwina zinthu sizinayende monga munayembekezera. Mwina mwabwerera ndi chikwama chokha. Koma musalole zimene mwataya zikupangitseni kuiwala zimene mungathe kukhala.
Yambani ndi sitepe imodzi. Yambani ndi luso limene lingakutsegulireni zitseko za ntchito, bizinesi, ndi kudziyimira pawokha.
π Pezani licence yanu ku Atuweni Driving School!!
Tsogolo silimamangidwa ndi zomwe munali nazo dzulo, koma ndi zomwe mukuyamba lero.
π 0999 175 469 / 0889 679 719