Nzeru App

Nzeru App Nzeru is an android app for Malawian teachers and students, it has thousands of documents.

Mayeso a Maneb akhala akutuluka within a week,  amene simupanga bwino osataya mtima, go back and do it again, kumbukiran...
29/08/2026

Mayeso a Maneb akhala akutuluka within a week, amene simupanga bwino osataya mtima, go back and do it again, kumbukirani madera onse omwe amakuvutani, ndipo focus on them.

Kwa omwe mukukalowa form 4, osadikira term three kuti muyambe kulimbikira, yambani leroli,

Ma resources ndi ofunika, Nzeru App inapangidea kuti ophunzira muzipeza zonse mosavuta, mosadikkra wina akuganizireni.

Link ya nzeru app ndi iy https://play.google.com/store/apps/details?id=com.codestar.mphunzitsiwanga

Mukukonzekera kukatsitsa ma points? Verani iziPewani izi:Kugwirisa ntchito notes zomwe mmalemba nokha kale.Pewani anzanu...
28/08/2026

Mukukonzekera kukatsitsa ma points? Verani izi
Pewani izi:

Kugwirisa ntchito notes zomwe mmalemba nokha kale.

Pewani anzanu onse omwe mumachita nawo zibwana, ngat ndikotheka pitan kutali ndi iwowo.

Tolerani mabuku, notes, ma pat papers ambiri zeeeeeedi.

Pangan download Nzeru App link ndi iyi https://play.google.com/store/apps/details?id=com.codestar.mphunzitsiwanga

osadikira mayeso afike, mukukalowa 2 kapena 4, yamban pompano, kuwerenga, kusova, Nzeru app ndipoyambira
23/08/2026

osadikira mayeso afike, mukukalowa 2 kapena 4, yamban pompano, kuwerenga, kusova, Nzeru app ndipoyambira

Address

Sandton
2038

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Nzeru App posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share

Category