Sir Emmanuel Jumbe

Sir Emmanuel Jumbe Tayambaso ndi 9 points 2025 MSCE EXAMINATION RESULTS. More than 80 students are from 9 to 20 points. Kuphunzila pompa pa online osalowaso mkalasi.

Inuso ndizotheka yambani nafe kuphunzila lero,follow this page. Call 099 606 9997/ WhatsApps 0991919328

03/06/2026

Azanu tikupanga final touches and Theory Examination coachings

Call
099 606 9997
099 606 9997
099 606 9997

Muli nako kale aka????Call or WhatsApp 099 606 9997099 606 9997Emmanuel Jumbe Include yodulira
03/06/2026

Muli nako kale aka????

Call or WhatsApp

099 606 9997
099 606 9997

Emmanuel Jumbe
Include yodulira

28/05/2026

mayeso ya chichewa

55 marks

Yankhani Zilapi zotsatirazi

1. Sakula koma akafa
2. Kakadakhala Ka mpeni kakadatintha
3. Mukagula ine mwagula misala
4. Simfumu koma mwini Sitilo
5. Sindine bambo kapena Mai
6. Pamene kaimapo ngati kagwa
7. Tudzi ta nkhalamba sititela tchetche
8. Amfumu alira powamvula chisoti
9. Akazi amakono ataya Ufa osaphika
10. Thileni madzi ndipitaso
11. Penya Uko nditole

27/05/2026

Tamaliza topic ya Differentiation

πŸ”₯πŸ”₯πŸ”₯πŸ”₯πŸ”₯πŸ”₯πŸ”₯πŸ”₯πŸ”₯πŸ”₯πŸ”₯πŸ”₯πŸ”₯πŸ”₯πŸ”₯πŸ”₯πŸ”₯πŸ”₯πŸ”₯πŸ”₯πŸ”₯πŸ”₯

Maneb zikubwera izizi Ndipo amadalira

27/05/2026

Alipo amene sadajoine official group pano??

Alipo amene ma practical sadakupezeni mpaka Pano? Mukupangatu chibwana mwina mukufuna mudzabwereze chaka cha mawa.

Call
099 606 9997
099 606 9997
099 606 9997

Azanu akuphunzila zobwera pamayeso zokhazokha

πŸƒπŸ½β€β™‚οΈπŸƒπŸ½β€β™‚οΈπŸƒπŸ½β€β™‚οΈπŸƒπŸ½β€β™‚οΈπŸƒπŸ½β€β™‚οΈπŸƒπŸ½β€β™‚οΈπŸƒπŸΎπŸƒπŸΎπŸƒπŸΎπŸƒπŸΎπŸƒπŸΎπŸƒπŸ½β€β™‚οΈπŸƒπŸ½β€β™‚οΈπŸƒπŸ½β€β™‚οΈ

Inu a form 3 yambani panopa kuphunzila muyambila poyambilira penipeni pomwe tidayambila

26/05/2026

Maneb pakubwera mafuso apapa Ndipo amapakonda

Call

099 606 9997
088 11 53 203
Emmanuel Jumbe
Include yodulira

Ngati mwawerenga tiyeni Nazoni yankhani Call 099 606 9997099 606 9997
25/05/2026

Ngati mwawerenga tiyeni Nazoni yankhani

Call 099 606 9997
099 606 9997

Address

Pretoria

Telephone

+265996069997

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Sir Emmanuel Jumbe posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The School

Send a message to Sir Emmanuel Jumbe:

Shortcuts

Share

Category