Ticondane Lemeka Letico

Ticondane Lemeka Letico

Sports updates

Operating as usual

25/07/2022

You all welcome!!

25/07/2022

Muzive kulandilidwa!

24/07/2022

Ndinayamba zau Coach zaka cha 2010 moti thawi imeneyo ndika coach komaso kumamenya nawo komano nditafika chaka cha 2013 ndinasiya zampira moti even kupeza anthu akumenya mpira palibe chikandisangalatsapo ndingoti sindimkaoneraso mpira .Komano mu 2014 nditalemba mayeso a standard 8 ndinapita pa Community ground kumene kunali game ya Red Lions komaso Big Bullets ndipo ineyo ndinapitako cfukwa azanga omwe ndimkacheza nao anali ndi game ya kalambulira bwalo yomwe inamenyedwa 12:30pm ndipo anabwera anthu osakwana mpakana ineyo ndinamenya nao ndipo ndinamenya team ya Tour bullets timkamenya ndi Zomba city kuchokera pamenepo ndiyambiraso za mpira mpakana Coach tour anandipasa u Captain komaso ndinayamba kumakocha Tour bullets U12 moti muchaka cha 2015 kumayambiliro ndinayambisa team yanga yomwe inali Young Bullets inali U10 pamenepo ndili form 1 tili mu June kunayambika League pa bwaila primary school ground ndipo team yanga inathera position 1 anthu anayamba kumandiuza kuti ndilindi ana abwino ndipo pamenepo ndinasiya kumenya Tour bullets ndimamenya Young shooters yomwe inali team ya mudzi mwathu kwa chidzalo ,Zomba ndipo coach wanga amkandiuza kuti team ndiisithe dzina ikhareso Young Shooters komano ndimakana moti tinasiya kuvana mpakana team ija l mean yanga ija inasokonekera ineso ndinayamba kukamenya Sammy Bullets yakwa Chikanda ndinalitu Goalkeeper ndiyeno kumayambikatso league ya U12 chaka cha 2016 team yanga ija inayambiratso komano ana ena anayamba ma team ena komano tinamenya League mpakana kuthera position 2 ndipo munthu wina amabwera kumazaonera ma games anandiuza kuti man mulindi luso ana anu akumenya bwino komaso inuyo mukuwalimbikitsa bwino ndipo Mulimbikire muzakharatu Coach odalilika ndinangoseka ndikumuuza kuti ndikuvani man nditafika chaka cha 2017 kunabwera League ya U14 yomwe amkapangitsa anali ZIMA College ineyo team yanga ndinaisitha zina from Young bullets to Fc Letico ndipo League imeneyo tinathera position 2 tinaluza ku final .continue .......

24/07/2022

Thanks all! Amene mwapanga like page yanga.

Want your school to be the top-listed School/college in Zomba?

Click here to claim your Sponsored Listing.

Location

Category

Telephone

Website

Address

Zomba
Zomba
Other Zomba schools & colleges (show all)
Mubarak Complex College Mubarak Complex College
Mubarak Complex College, P. O Box 1058 Zomba
Zomba

RECOGNIZED & REGISTERED by the Malawi Government through TEVETA, located in Zomba township.

Drepar community day secondary school Drepar community day secondary school
Zomba

Located in Zomba district, in maluwa villagw close to bulaymana primary scholl

Sir Alfred Sir Alfred
Zomba
Zomba

SCIENCES

Nyasa Voice Education Centre Nyasa Voice Education Centre
Zomba-Malosa (Opposite Chilema Post Office)
Zomba, 265

We are the only source of hope to Malawian youth. Free short course trainings, full time enrolment.

Essenberg Montessori School Essenberg Montessori School
Chinamwali , Habitant
Zomba

Essenberg montessori pre-school offers an individualised and safe learning Environment that responds

Spark Liko Spark Liko
Zomba, 265

Rapper & Singer

Nyasa Voice Secondary Education Centre Nyasa Voice Secondary Education Centre
Zomba

A centre for quality education spiced up with free entrepreneurship and technical training ..we are

Malawi chills and charts and news updates Malawi chills and charts and news updates
Hopenkhulembe@gmail. Com
Zomba

Domasi institute of management and technology Domasi institute of management and technology
Zomba

A technical college located in zomba at a trading called domasi works. offers both vocational and e

Mphunzitsi wa Chingerezi Mphunzitsi wa Chingerezi
Zomba

This page is created to help directing those people who either have never been to school or have bee