22/12/2023
KHOTHI LIMASULA CHIPHE: Khothi lamasula mtsikana opha mwana wake
Mtsikana wazaka 20 yemwe anamangidwa mu 2021 kamba kakupha “mwangozi” mwana wake wa chaka chimodzi ndi miyezi 9, lero ali ndi chimwemwe chodzadza tsaya pomwe wamasulidwa ndipo wauzidwa kuti asapalamuleso mlandu uli onse kwa chaka chimodzi.
Werengani nkhani yonse apa:
Mphatso: Khothi lamasula mtsikana opha mwana wake Malawi 24 | Latest News from Malawi | Stay up-to-date with the latest news from Malawi and around the world, 24/7.