Anzathu Pamalonda Network

Anzathu Pamalonda Network A membership-based B2B networking platform connecting small, medium, and large business owners, professionals, and aspiring entrepreneurs.

We facilitate meaningful business connections, foster referrals, encourage collaboration, and create opportunities.

17/09/2026

Why join Anzathu Pamalonda Network?

Connect. Promote. Learn. Refer. Collaborate. Grow.

Your business should not grow alone. Become part of a network of entrepreneurs and business professionals across Malawi where relationships can become referrals, referrals can become customers, and connections can become opportunities.

Grow • Market • Connect

MONGOKUMBUTSANAKodi mukukumbukirabe chifukwa chomwe munayambira kupanga bizinesi yanu, kapena mwaiwala? Nthawi zina ulen...
17/09/2026

MONGOKUMBUTSANA

Kodi mukukumbukirabe chifukwa chomwe munayambira kupanga bizinesi yanu, kapena mwaiwala? Nthawi zina ulendo wa bizinesi umakhala wovuta, koma ndikofunika kubwereranso ku cholinga choyambirira chomwe chinakulimbikitsani mtima. Musaiwale chifukwa chomwe munayambira pitirizani kulimbikira mpaka maloto anu akwaniritsidwe. Tisatayilire ndikuyiwara chifukwa chomwe tinayambira kupanga zomwe tikupangazo.



17/09/2026

SASKANI MALONDA GHINU KUPOLOTE MWA A.P.M

Ku wanthu wo wachita malonda ghamana-ghamana wangalembetsa ndikuja membala wa Anzathu Pamalonda Network

Gulu lidu kusele nkhwa wezi.

Yiwu wapeleka malunguchizgu gha kendeskelu ka Malonda ndipo mungakuzgiya business yinu.

Tumani email ku [email protected] kuti muvwi vinandi..

Meet Our Valued Member, Lush & LovelyLooking for fashion, beauty, gifts, and more? Lush & Lovely has you covered! They o...
17/09/2026

Meet Our Valued Member, Lush & Lovely

Looking for fashion, beauty, gifts, and more? Lush & Lovely has you covered!

They offer:
Clothes,Shoes, Bags, Electronics,Flowers,Chocolate Bouquets,Nails,Lashes, Hair Extensions & Braiding

They also deliver throughout Malawi via reliable couriers.

Available for retail and orders, subject to their terms and conditions.

📍 Find them at Zingwangwa Market
📞 0885 007 450
📧 [email protected]

Show some love and support our valued member of Anzathu Pamalonda Network.

17/09/2026

KODI MUMATSATSA BWANJI KATUNDU WANU?

Mukamatsatsa katundu kapena ntchito yanu, kodi mumawaudza chiyani makasitomala anu? 🤔

Kodi mumangowauza za zinthu zomwe katundu wanu ali nazo, kapena mumawafotokozera phindu limene angapeze akagula kapena kugwiritsa ntchito katunduyo?

Mwachitsanzo: M’malo monena kuti, “Sopo wathu wapangidwa kuchokela ku zomela zachilengedwe,” m***a kunena kuti, “Sopo wathu ndiwo pangidwa kuchokela ku zomela zachilengedwe, ndi wofewa pakhungu ndipo umakuthandizani kukhala waukhondo komanso watsopano opanda mankhwala owopsa.”

Kutsatsa bwino sikungokhala kuuza anthu zomwe katundu wanu ali nazo. Ndikuwonetsanso chifukwa chake katunduyo ndi wofunika kwa iwo komanso vuto limene ungawathetsere.

Tikufuna maganizo anu pa nkhaniyi.

Mukamatsatsa katundu kapena ntchito yanu, kodi nthawi zambiri mumawauza chiyani makasitomala?

Kodi katunduyo ndi chiyani?

Zinthu kapena maonekedwe ake?

Phindu limene kasitomala amapeza?

Vuto limene katunduyo amathetsa?

Kapena mtengo ndi phindu limene kasitomala amapeza akagula?

Tiuzeni mu ma comment. Tiphunzire kwa wina ndi mnzake kuti tithandizane kukulitsa luso lathu lotsatsa ndi kuyendetsa mabizinesi athu!

17/09/2026

ADVERTISEMENT TIP!

When you advertise your product or service, what do you focus on?

Do you simply tell customers about the features of your product, or do you explain the real value and benefits they will get from using it?

For example: Instead of saying “Our soap contains natural ingredients,” could you say “Our natural soap is gentle on your skin and helps you feel fresh without harsh chemicals”?

A good value proposition is not just about telling people what your product is. It is about showing them why it matters to them and what problem it solves.

Members of Anzathu Pamalonda Network, we want your answers!

When advertising your product or service, what do you normally tell your customers?

What the product is?

Its features?

The benefits to the customer?

The problem it solves?

Or the value the customer gets from buying it?

Share your experience in the comments. Let’s learn from one another and improve the way we market our businesses!

Timve nawo.

17/09/2026

Lero tikambilana zokhudzana ndi Value Propostion.

17/09/2026

Mwadzuka bwanji? Tiyeni tichedze lero.

Calling all College & University StudentsAre you running a small business on campus? This one's for you! We're inviting ...
14/09/2026

Calling all College & University Students

Are you running a small business on campus? This one's for you!

We're inviting students from all university campuses in Malawi (Private and Government) to join our upcoming Zoom Webinar, where you'll learn directly from experienced business gurus on how to grow, sustain, and scale your campus business beyond graduation.

Whether you're selling snacks, doing hair, printing assignments, reselling airtime, or running any other campus hustle this webinar is designed to help you take your business further and turn it into something that lasts long after you leave campus.

Date: 24th September, 2026 Time: 6:30pm-8:00pm Platform: Zoom

FEE: MK5,000.00/ Student.

Who should join: Any student running a business on their campus

Stay tuned for more details, and get ready to learn, grow, and connect.

THEME: Started On Campus, Built for the Future.

11/09/2026

Mwakhalapo ndi kale pa bench koma simunampase moni kasitomala wanu anakugulani mu June. aaagh inu, asamaleni akasi!

Address

Nkhata-bay, Nkhata Bay
Mzuzu

Telephone

+265888813814

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Anzathu Pamalonda Network posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share