Ntengatenga News

Ntengatenga News

Share

ZAMABOMA TV & RADIO 📻

Photos from Ntengatenga News's post 13/07/2026

Kwinaku anthu ati atukwana 🙄🫩akuti akuteteza munthu awapeza pakwao amangogona ku baracksiko ndiye lero muti chani inu a army Kod 🥺

Photos from Ntengatenga News's post 11/07/2026

Upile macheka arrested in Ntcheu on very serious charges

CHICHEWA translation

Upiletu wazaka 19 anapeza chibwenzi ndithu madala andalama zake , pwepwete Oti mamawa Iwowo tea amamwera sausage . Chinyumba cha Mamunayu ngati Cha Inspector General wa Road Authority.Pwepweteyu amakhala Ku Mozambique .Ndipo iyeyo akhala akupanga plan kuti Ameneyu nditani kuti ndikhaliletu madam .

Upile anaiwerenga ndipo anapita dala mozipeleka kwa bamboyu kukalandila ubatizo wa Mbokshen ndipo atatero anabwelela Ku Ntcheu nkuyamba kumuuza kuti Ali ndi mimba.

Apa bamboyu anazimva mphamvu, gluco, Illovo komanso Barracks kuti iye ndi akamuna achinya chigoli. Masiku atayandikila Upile anamuuza Mamunayu kuti Ali ndi Mwana ndipo Dzina lake Beauty. Apa ndiye madala anaika nyimbo ya Ndombolo ya solo Kwinaku akumvela ma headphone nyimbo ya Lulu ya "Ana ambiri mbiri bwanji nzalera" .

Kenako Bamboo anaitanisa Upile kuti akamuone Mwana . Apa upile BP inakwera. Bamboyo anamuuza kuti Wamukonzela phwando apa Upile Mtima unazunzika

Kenako Upile anapita kwa best friend wake kwa kampepuza amene anali ndi mwana mnkumasewera naye Kwinaku akumubeleka paja mwana wanzako ndi wako yemwe umatha kudya naye.

Kenako anamuuza nzake kuti ndikupita kunsika ndi mwana ndikubwera. Nthawi yomweyo anatenga mwana nkuthawa naye Ku Mozambique kuti akamuonese kuti Beauty uja ndi uyu ndipo wakutengani Nkhope yonse ......yao ija azimai . Mwini mwana atazindikila anapita Ku Ntcheu Ku police .

Page ino tamuwalisa Upile kuti mumuone bwino. Tachotsa chifunga

Police ya Ntcheu itamva inatenga call log popanga browse ESCOM, Malawi Railways, FAM, Mining Authority, COSOMA ndikuona Upile Ku Mozambique apa Police inatsatila nkonko pogwilitsa ntchito Zida zoophya monga Aircons, Bullet proof, Toll gate, ma Drones, EGENCO transformer ndikumumanga
Pano Ali Ku Ntcheu police ndipo wavomera mlandu

Photos from Ntengatenga News's post 11/07/2026

Justice for Dr. Atughanile Chomo. 💔

A life dedicated to saving others was taken far too soon. My heartfelt condolences go out to her family, friends, colleagues and everyone mourning this tragic loss.

May the truth come to light, may justice be served and may her soul rest in eternal peace.🕊️

11/06/2026

Whatsapp number 0881872081

10/06/2026

msce candidates ka nthawi ndie katsara kochepa tipezeni ku inbox kwathu tikupangeni ku ma group a Whatsapp anthu msce final touches

21/05/2026

2026 MSCE Exams are around the corner, inbox us to be added in 2026 msce practical Whatsapp group. this group is only focusing on how to answer practical msce papers and discussing some mock from different schools follow us for more info

15/04/2026

Shout out to my newest followers! Excited to have you onboard! Elias Mantchondo, Samuel Henr Mangani, Amon Kamanga, BØÍ MÍSHÖ, Pilirani Kamisa, Davie Ciwale, Don Ziwiri, Wambone-amasile Asigele-wachabepe, CRAĪMZÉR KÅMOWA, Nafe Nafe, Collings Bandah, Charles Blessings Mangondo, Chimwemwe Laughter Chimwala, Josophat Chazungu MW, Herbert Mandina, Joel Lee Mundy, Trizah Jonny, Poul Paulos, Wyson C Muzuwele, Marcus Rashford, Ficky Thuq, Grespar Matter, Paui Partison, Kelvin L Dany, KIDD CHIPOLO, Chipiliro Ezra, Skyler Kamanga, Namitoso F P School, Ly Gift, Blessings Kamoza Nyasulu, Hellington Precious, Mayamiko Sichali, Brave Msowoya Brave Msowoya, Patra Mwaikera, Elimond Kaleso, David Khemboh, Gilbert Simon, Memori Chimombo, Deborah Pinifolo, Owen Chimphangu, Aciah Zuze, Foster Charles Banda, Mphatso Grey, Innocent Petro, Tionge Banda, Richard Kamwachale

Want your school to be the top-listed School/college in Mpemba?

Click here to claim your Sponsored Listing.

Location

Category

Website

Address

Mpemba