Shadreck yahaya

Shadreck yahaya am a Muslim

a Head ndi zizukulu
06/06/2026

a Head ndi zizukulu

Chips chilipobe?
03/05/2026

Chips chilipobe?

23/04/2026

Marriage is allow in Islam and is also farila and sunna

19/04/2026

Ndiwa sabath

Family πŸ«‚πŸ‘¨β€πŸ‘©β€πŸ‘§β€πŸ‘§
11/04/2026

Family πŸ«‚πŸ‘¨β€πŸ‘©β€πŸ‘§β€πŸ‘§

10/04/2026

Pazifukwa zina kwa anthu ongolonjeza koma osaonetsa kusintha zinthu posazindikira kuti kumabwera wina oposela iweyo umagwa nawo udindo oti unali wako
in 2030 choose wisely

Eid Mubarak
21/03/2026

Eid Mubarak

Eid Mubarak family
20/03/2026

Eid Mubarak family

15/03/2026

Tsiku la Qiyāmah Kukavuta.

Allah akamuwuza munthu awerenge yekha buku lake, ndipo kapolo akalakatula zonse anali kuchita .
kenako Allah azati kwaiye:

β€œE iwe kapolo wanga, kodi angelo anga olemba ntchito (al-kiram al-katibΔ«n) anakupondeleza polemba chinachake comwe sunachite?”

Munthuyo adzayankha:
β€œAyi Mbuye wanga.”

Kenako Allah akati:
β€œKodi pali chilichonse ungakane mu zomwe ukuona (m’buku la zintchito zako)?”

Iye adzayankha:
β€œAyi Mbuye wanga, palibe ndikuka.β€πŸ˜­

Kenako pakamwa pake padzatsekedwa, ndipo ziwalo zake monga manja, mapazi ndi khungu lake zidzayamba kulankhula kufotokoza kuchitira umboni zomwe ankachita pa dziko lapansi.

πŸ’”πŸ’”πŸ’”πŸ’”πŸ’”πŸ’”
copy and paste

ukupanga zofoila iweyoπŸ˜ƒπŸ˜ƒπŸ™Œ
14/03/2026

ukupanga zofoila iweyoπŸ˜ƒπŸ˜ƒπŸ™Œ

Address

Chowe Fp School Box 51
Mangochi
MANGOCHI

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Shadreck yahaya posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The School

Send a message to Shadreck yahaya:

Shortcuts

Share