Riaz Chitukuko Official

Riaz Chitukuko Official Educator. Mentor. Explorer

25/02/2026

Mbalame ku Kazakhstan kuno mu winter zimasowa .

Pemphero mphande akapanga post galimoto yake ndiye Congratulations,Ine kupanga post yanga matama ett ? aMalawi mukhalike...
20/02/2026

Pemphero mphande akapanga post galimoto yake ndiye Congratulations,
Ine kupanga post yanga matama ett ? aMalawi mukhalike 😂🙌🏽

Follow me guys 🫡

Kwachichela mwa mkokomo
19/02/2026

Kwachichela mwa mkokomo

19/02/2026

Iyi si mvula, ndi Snow ameneyu.
Kupangila anzathu aku Mangochi inu 😂

Mukapeza nthawi, kafiken pa Liwonde National Park .
18/02/2026

Mukapeza nthawi, kafiken pa Liwonde National Park .

Malape Pillars ndi miyala yayitali yomwe ili m’boma la Machinga .Mbiri, Miyambo ndi ZikhulupiriroKwa akuluakulu akale m’...
17/02/2026

Malape Pillars ndi miyala yayitali yomwe ili m’boma la Machinga .

Mbiri, Miyambo ndi Zikhulupiriro

Kwa akuluakulu akale m’dera la Machinga, Malape Pillars ankawawona ngati:
• Malo opatulika
• Malo okhala mizimu
• Malo amene anthu amamva mawu osawoneka kapena kuwona zinthu zachinsinsi
Choncho achinyamata samaloledwa kupita popanda chilolezo cha akulu akulu .

Masiku ano, Malape Pillars akudziwika ngati:
• Malo okopa alendo (tourist attraction)
• Malo ochitira maulendo a mapiri (hiking)
• Malo ofunikira pachikhalidwe ndi pa chilengedwe cha Malawi

Recommendation:
Ndizofunika kupeleka value ndikusamalira malowo kuti azithandiza pa zachuma ndi kuteteza chikhalidwe.

Zochitika ku Machinga .Apolisi ku Machinga ati akusakasaka anthu awiri omwe akuwaganizira kuti apha bambo wazaka 38, a F...
17/02/2026

Zochitika ku Machinga .

Apolisi ku Machinga ati akusakasaka anthu awiri omwe akuwaganizira kuti apha bambo wazaka 38, a Fred Ligomeka, atawapeza akuba nkhuku panyumba ina m'bomali.

Mneneri wa polisi ya Machinga, a Western Kansire, ati a Ligomeka usiku watha anapita kukaba nkhuku ku nyumba ya munthu wina m'mudzi mwa Lipagani.

Iwo ati mwini nyumba atazindikira kuti kwabwera wakuba anayamba kukuwa zomwe zinadzutsa khwimbi la a anthu n'kugwira oganirizidwawa nkuyamba kuwamenya.

A Kansire ati kutsatira kumenyedwaku oganiziridwawa anavula kwambiri ndipo anatengeredwa kuchipatala cha Chikwewo, komwe achipatala atsimikiza kuti afa kaamba kotaya magazi.

A Fred Ligomeka amachokera mudzi mwa Mwikawa mfumu yayikulu Ngokwe ku Machinga

(Copied)
Side note : tisiye kuba

MACHINGA Malawi 🇲🇼
15/02/2026

MACHINGA Malawi 🇲🇼

15/02/2026
15/02/2026

Hello. Ine ndi Riaz waku Machinga , page iyi ndiyanyuwani ndipo izikhala ikupanga focus zochitika zambiri zaku Machinga komanso zina zosiyanasiyana. Ngat ingakupezen, pangan FOLLOW.
Be the first to follow and let’s normalize UNITY.

Address

Chikweo
Machinga
P.0 BOX 69

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Riaz Chitukuko Official posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share

Category