03/02/2026
Kodi mufuna mutachita upgrade certificate ya MSCE yanu,, koma kamba k**a busy mukuona kuti loto lanu silitheka? Tipezeni ife a Mindwave Online School tikuthandizeni ndima Phuzilo anthu apa phone ya m'manja pogwiritsa nchito WhatsApp basi..
Inu muziphuzila ma subject onse mumatenga aja panthawi imene muli free after work madzulo..
Kaya muli ndi ana oti akuvutika ku school akungobwereza! Musataye nthawi ndikumunyoza mwana yo mubwereseni kwa ife.
Fees : 10,000.00. pa Mwezi
Reg fee : 2,000.00.
Lowani! Lero! Ndipo muzakhoza bwino
0883 14 94 21