Chiyembekezo driving school

Chiyembekezo driving school IFE ACHIYEMBEKEZO DRIVING SCHOOL MALINGana ndikutseka KWA nseu pamatchasi tatsegula office INA pa k

27/10/2025

Chiyembekezo driving school inatsegulanso office ina pa katcom near chilinde market nde osadanda ayi mitengo yanthu ndi mommunja mosaboola mthumba and timalambikanso ndithu

IFE ACHIYEMBEKEZO DRIVING SCHOOL MALINGana ndikutseka KWA nseu pamatchasi tatsegula office INA pa k

27/08/2025

Chinsinsi chaku chiyembekezo timakambika nthuni

IFE ACHIYEMBEKEZO DRIVING SCHOOL MALINGana ndikutseka KWA nseu pamatchasi tatsegula office INA pa k

27/08/2025

Chiyembekezo driving school ma fees ake anakali omvelelabe inu kukwezako nde takweza koma sitingafanane ndi awo ndati awo!! tipezeni lelo pa kamuzu institute ndi pa katcom chilinde nkhani inenso ndiyakuti mumaloledwa kupeleka pang'ono pang'ono uku mukugaya machine

IFE ACHIYEMBEKEZO DRIVING SCHOOL MALINGana ndikutseka KWA nseu pamatchasi tatsegula office INA pa k

17/07/2025

Ma fees nde akwela koma akwela momvelela watsapp me kuti mumve zambili 0997638175

IFE ACHIYEMBEKEZO DRIVING SCHOOL MALINGana ndikutseka KWA nseu pamatchasi tatsegula office INA pa k

17/07/2025

Malawi wavuta koma ife timaganizilabe inuyo ma customer anthumpake kukweza kwanthu sikunagunde mthumba mwanu kwambili tapanga kuti aliyense akwanitse kuphunzila ndikumphunzitsanso ana ake ndipezeni pa watsapp 0997638175 ndipo ndi chiyembekezo driving school simudzakhalanso chimodzi modzi

IFE ACHIYEMBEKEZO DRIVING SCHOOL MALINGana ndikutseka KWA nseu pamatchasi tatsegula office INA pa k

Shout out to my newest followers! Excited to have you onboard! Rajabu K Salimu, Moffat Simbeyi Toast Mw, Friday Dada Tao...
08/02/2025

Shout out to my newest followers! Excited to have you onboard! Rajabu K Salimu, Moffat Simbeyi Toast Mw, Friday Dada Taombe

04/10/2024

IFE ACHIYEMBEKEZO DRIVING SCHOOL MALINGana ndikutseka KWA nseu pamatchasi tatsegula office INA pa k

04/10/2024

Mwayi wabwino Kwa nonse okhala dziko la Malawi! Ife Chiyembekezo driving school tatsegula boarding school yomwe idzilandila anthu azigawo zonse, musachedwe malowatu akulimbilana bcs ndiooneka bwino zedi zakudya zakenso zabwino osati dairy masamba ndi nyemba ayi, ngati mukufuna kumva zambili ndiimbileni pa 0997638175

IFE ACHIYEMBEKEZO DRIVING SCHOOL MALINGana ndikutseka KWA nseu pamatchasi tatsegula office INA pa k

23/07/2023

Chiyembekezo driving school inja osadzaiphweketsa!!! Uyende apa umva ndinaphunzila ku chiyembekezo ndikukamba za oyendetsa magalimoto a boma, ma organisation inu!!! Call me today kuti mumve zambili 0997638175

IFE ACHIYEMBEKEZO DRIVING SCHOOL MALINGana ndikutseka KWA nseu pamatchasi tatsegula office INA pa k

24/05/2023

Mukufunabe mutaphunzila galimoto koma mitengo ikukuwawitsani mitu ndipezeni ndithu ndipo ndidzakuchotselani ndipo simudzakhumudwa ndipezeni ndithu pa kamuzu institute

04/02/2023

February asakukanikitseni kukhala katswili oyendetsa galimoto tipezeni ife achiyembekezo driving school ndi 323,000 mudzaphunzila mpaka kutenga licence, 0997638175 tipezeni ndithu

02/01/2023

Kuyambila pa 1 January ma fees anthu tatsitsa kuti aliyense aphunzile manual ndikukhala ndichiphanso imene ili licence

Address

Chilinde
Lilongwe

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Chiyembekezo driving school posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share

Category