22/12/2025
CHONDE SAMALANI part 1
N'buyomu tinadzafotokoza nkhan ya mnyamata wa ku kasungu mene analowera satanic koma sitidaimalizitse tikudikila mwiniwake chifukwa amati adzakhale live pa Apezeri
Pano tabwera ndi nkhani ya mnyamata wina waku salima amene anakumana ndi tsoka lobwera ngat mwayi
π Dzina langa ndine Joseph ndimakhala ndimakhala ku salima ineyo ndinkapanga business yogulitsa mtedza okazinga kumapita nawo ku magalimoto k*t anthu atigule tsiku Lina ndinakazinga mtedza wanga ulendo pa msika
Ndinagulitsa mtedzao kenako kunafika galimoto ya juke munali Mzimai mmodzi yekha basi ndek*t anandiitana k*t ndikamugulire Madzi a sealed ndinapita kukagula ndinawapatsira anandipatsa ndalama yokwana 2000 ndinathokoza anapita posakhalitsa kumadutsa Mtsikana nkugwetsa pes yake ine nk*tola kumupatsa tsiku ilitu ndi limodzi zimachitika zosezi
Kenako anatenga 2000 nkundipatsa nkundiuza k*t mwayi wako ndiwa lero kenako a kupita nde amalowelaso komwe kunalowera galimoto ya mayi aja chaku nkhotakota tikafika pa kaphatenga paja nde kumalowaa cha ku nkhotakota nde chodabwitsa atayenda mtunda wa 50 meters ineyo mtima unangong'ambika kuyamba kumangotsatila
Nde ndinkangotsatila kumangoyenda koma mkazi uja sanacheuke ayi kumangopita ineso pambuyo mpaka mtunda wa 1 kilometer
Kenako anandidikira ππππππππ
Nkundiuza k*ti ndiwe olimba mtima
Pangani follow πππ Vattkan
Tikupatsilani nkhani yose koma mwa MA part chifukwa ndiyaitali kwambili pangan follow k*t zisakuphonyeni