04/08/2026
Eh koma ana awa atakulileko! Ife computer mouse tinamudziwila ku University koma awa ayamba kale kuchita zodabwitsa pa computer! Send your kids to the Digital Discovery camp 2026, Maphunziro ayamba kale this week ku Kairos Training Center ku Limbe and will be happening 3 days in a week for the next 4 weeks. 0881 23 99 55 for more.
04/08/2026
Maphunziro awa ayambika lero, malo atsala ochepa ngati mukulingalilabe lembetsani mwachangu muwajoine amnzanu.
04/08/2026
Amangwetu, lero tiwanyadile ma single mothers omwe akuchilimika paokha kuti ana awo adye and achite bwino, mumakwana inuyo, Mulungu akupatseni chisomo chokwanila
03/08/2026
Testing testing, kukonzekela kulandila ana for the Kids Digital Discovery Camp at Kairos Training Center this afternoon, akondeni ma bundle of joy anuwo😄😍....Ena akuona ngati AI, ayi ndithu Amangwetu
03/08/2026
Amangwetu, "Pakuti Malembo amati, Aliyense wokhulupirira Iye sadzachita manyazi." (Aroma 10:11) Drop one word if your trust is in the Lord!....mwadzuka koma inuyo?
02/08/2026
Quarter to Greatness! Ma training omwe timawayembekezera Aja akuyambika mmawa: Electrical Installation, Phone Repairing & ICT. Let's meet @ Kairos
02/08/2026
Amangwetu, ife lero tinakapemphela tabwelako, tione mmene inu munatchenela lero 🙂
02/08/2026
Koma akanati bwelani ku stadium mudzalandile ma K1million ndiye zima juzi kuno, apa tiyeni Ku church iiih ayi kwazizila, aah amangwetu osamatelo tatiyeni😃
01/08/2026
Amangwetu, ngati mumawanyadila taponyani pic ya okondedwa anuwo Tione olimba mtima😄😍, Nambo adyimwiche dyamani?
31/07/2026
Amangwetu Kodi stage ya kwanu mumaitchula kuti chani? Koma mwadzuka bwanji?