17/07/2025
Esau anangulitsa ukulu wake chifukwà cha njala ,,,azitumiki Amulungu tisangulitse ukulu wathu chifukwa cha anthu awa amachedwa ma politicians,,,amatifuna nthawi ya campaign koma zikawathekera amatiiwala ,,,,tiyeni campaign yayambikayi ifenso tipange campaign ya Yesu ,,,tisaiwale kuti Yesu akubwera ,,,ma politicians tisawanamize kuti tidzawavotera cholinga mungowadyera ndalama zawo ,,,nkhalani anthu achiyero ,,
Kwathu sipadziko
Ambuye akudalitseni pamene mukupanga nanu campaign ya Yesu
Zikomo