Apostle Davie itt Luckson

Apostle Davie itt Luckson RIVERS OF LIFE INTERNATIONAL 🌍β›ͺπŸ“–

"The seed of salvation"

Ndi pemphero losweka mtima Mulungu anamva nampasa Hana umboni,NDIKUPEMPHERA Mulungu amve kulira kwa mtima wanu nakupasen...
23/08/2026

Ndi pemphero losweka mtima Mulungu anamva nampasa Hana umboni,
NDIKUPEMPHERA
Mulungu amve kulira kwa mtima wanu nakupaseni umboni

Lero Mulungu achotse ⛓️‍πŸ’₯ Matemberero, Masoka ndi Minyama pa moyo wanu mu dzina lamphamvu  Yesu
23/08/2026

Lero Mulungu achotse ⛓️‍πŸ’₯ Matemberero, Masoka ndi Minyama pa moyo wanu mu dzina lamphamvu Yesu

22/08/2026

Onse ofuna kukhala nafe pa WhatsApp group Link ili mu comment section πŸ‘‡

Mulungu wanga,Chonde lero tonthozani mwana wanu uyu emwe akudutsa mu ululu, akufunika chikondi chanu chodabwitsa, chitan...
22/08/2026

Mulungu wanga,
Chonde lero tonthozani mwana wanu uyu emwe akudutsa mu ululu, akufunika chikondi chanu chodabwitsa, chitani champhamvu pa moyo wake ndi kuzionetsera kuti ndinu Mulungu

22/08/2026

Anthu amene anakunyozani chifukwa cha kusowa mwana posachedwa abwera kudzakondwerera umboni wanu odabwitsa, mu dzina la Yesu πŸ™

Mulungu akuchiritseni Kwatunthu mu ululu umene mukudutsamo lero
22/08/2026

Mulungu akuchiritseni Kwatunthu mu ululu umene mukudutsamo lero

22/08/2026

NDIKUPEMPHERERANI
Mwana wanu akhale opambana pazonse ndi kukupangani kukhala onyadira mu dzina la Yesu

Ndikufuna kukuuzani kuti simuli nokha mu vuto limenelo, Mulungu ali nanu ndipo akuthandizani kutuluka mu ululu umenewo
22/08/2026

Ndikufuna kukuuzani kuti simuli nokha mu vuto limenelo, Mulungu ali nanu ndipo akuthandizani kutuluka mu ululu umenewo

Atate,Ndikupempherera iwo amene akufunafuna ntchito ndi chochita chokhazikika, chisomo chikhale pa iwo ndi kukhuza mitim...
22/08/2026

Atate,
Ndikupempherera iwo amene akufunafuna ntchito ndi chochita chokhazikika, chisomo chikhale pa iwo ndi kukhuza mitima ya olemba ntchito kuti awakumbukire mu dzina la Yesu.

Usiku uno ndi usiku wanu wotsiriza kulira ndi kuda nkhawa za mavuto anu, Mulungu akukuchitirani chozizwitsa!!
21/08/2026

Usiku uno ndi usiku wanu wotsiriza kulira ndi kuda nkhawa za mavuto anu, Mulungu akukuchitirani chozizwitsa!!

Address

Machinjiri
Blantyre

Telephone

+265882675819

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Apostle Davie itt Luckson posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The School

Send a message to Apostle Davie itt Luckson:

Shortcuts

Share

Category