MSCE online classes

MSCE online classes aiming at producing best academic performance learnt at NRC college,

05/12/2025

Hello fam

15/12/2024
15/12/2024
18/08/2024

Ndege ina mudali anthu Andale okha-okha (politicians), itauluka ndegeyi idaluza engine zomwe zidapangitsa kuti ndegeyi igwe ndipo malo ogwera ndegeyi kudali ku farm, mwini farm yu ataona kuti ndege yagwa adathamanga ndi omuthandizila ntchito ake ku malo angozi-wa, atafika pamalopa adaona kuti ndegeyi idali yodzadza ndi andale.

Mothandizana ndi anthu ena a ma farmer oyandikana nawo adakumba chidzenje chachikulu ndi kukwilira anthu onse amene adali mu ndegeyi, a police atafika adangopeza ndege yokha ndipo adafusa mwini farm koma iye adayankha monyadira kuti "takwilira mitembo yonse"

A police: Koma munaonetsetsa kuti onse ndi omwalira panalibe amoyo?

Mwini farm: Ndizotero ndithu onse anali omwalira, ngakhale enawo amakuwa kuti "musatikwilire sitidafe" koma ife sitidakhulupilire mudziwa ma politicians amanama nde mosataya nthawi tangokwilira onse.

14/08/2024

Address

Bangwe
Blantyre

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when MSCE online classes posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The School

Send a message to MSCE online classes:

Shortcuts

Share